
SONG
Ndizakukwatira (Prod. APEE)
Giboh Pearson · Ndizakukwatira · Prod. Apee · Local
DL 35,024 downloadsST 2 streams
TRACK DETAILS
Song information
ArtistGiboh Pearson
AlbumNdizakukwatira
GenreLocal
Length4:31
File size6.3 MB
FormatMP3
Track1 · Disc 1
Year2022
LabelPhalombe Music
Added to Malawi Music1 Jun 2022
Downloads35,024
Streams2
Rating3.4 / 5 mics · 32 ratings
MORE FROM THE ARTIST
View artist →More songs by Giboh Pearson
COMMUNITY

Enter Comment AGIBO ZABWINO
Zambian
koma chino chakaa ndizakwatii
hit from gibboh pearson
Oweee
Nice music
Bashiri
Good songs and meaning songs
Mumakwanila abwana
Mumatha abraz
AKUYESESA AGB MUMAKWANILA
giboh
Mr giboh mmatha ili boh kwambiri
Mwaphaaa????
Nice man ndzakukwatria kma mochedwa
Your fun here
In Lilongwe
Well done
Mwatodza
Well done
Nyimbo Ili bho
Wapha
Ndizakukwatila koma mochedwa ilibho kwambiri
Nyimbo ili bhooo ndipo Agibho mmanditsuntha mmaganizo
Zili boh anjira.
Nyimbo ili ?kuinjoya bs
Mbambande Ili nyatwa hvy
Umatha ase uli super
Wapha asee
Uli faya brosk bg up
Lovely song
To those who are saying this track is mbola. Guys ndinu a nsanje!!!!
Umatha ase
Koma Gibo umatiimilira aisy, phalonbe yonse wainyamula.
Ndikudzakwatira
Ndikudzakwatira
Iyi mwaimilira man mupitilize kutipasira nyimbo wabwino
Mwapha man
Nyimbo mwapha man
Kali bho
Inuyo munabwera kuzakhala mumatiimilira
Giboh koma musamalenayetu
Wampha
Gibo analembetsa kale dzina mu oyimba aku malawi....Gibo ndiwe bigman aise umapha
Umatha adha
Nic
Ili khenge
This hit is lit
Giboh ndi one
Mwapha broh
Naa iwe kulumikiza ma liwu umatha koopsya.
Mesa ndimakufila nanga
Umatha iweyo my inlow
Umakwana mulopwana
Mumatha a King cha adad
Wakwathu iwe umapha not kutha wow
Munthu oipa pa sound Mr phalombe music ndiwe asset wanga. Mmmmm mukuswa sound #asakaonde ndikulira #avala velo
Mr gibo uremu wanu mesaa inu nd 1
Khenge
Excellent
Gibo iyo ndi one ndimakufila hrvy man umadziwa kuimba ngati siwe wakuphalombe nfipo umaimilila phalombe yonse brooooo big up