
SONG
Galu Ndine (Prod. Tricky Beats)
Giboh Pearson · Galu Ndine · Prod. Tricky Beats · Local
DL 35,570 downloadsST 7 streams
TRACK DETAILS
Song information
ArtistGiboh Pearson
AlbumGalu Ndine
GenreLocal
Length4:33
File size6.6 MB
FormatMP3
Track1 · Disc 1
Year2024
LabelPhalombe Muzik
Added to Malawi Music22 Mar 2024
Downloads35,570
Streams7
Rating3.6 / 5 mics · 58 ratings
MORE FROM THE ARTIST
View artist →More songs by Giboh Pearson
COMMUNITY

Enter Comment
Enter Comment
Enter Comment
Inuyo munabwera kuzakhala wathuwathu Gibo.
1
Ndamukonda Gibo pearson amayimba bwino
Nyimbo yosangalatsa
Nice song ?
Giboh pearson inuy mumakwana kwambiri kms mudafika ife kuno timakond kuvelel nyimbo zanu agiboh "mbambande."
Mumandvesa kukoma komanso kundpangsa kutchuka ndkapta kumpoto makamaka mukamat PHALOMBEx2 MUSC Boma la2 mumalika mamap abraz pitilizan ktvesa kukoma osafoka ine ndl pambuy panu NEVER GV UP
Takulandila kuno kumalawi
Auperb
UMAKAWANA
Malumewa anabweratu shaaaa mbambande
Umakwana
Enter Comment: nyimbo zaci malawi ndi mazikonda kwambiri-mbiri. Komanso zivuta ucita download.
Njira ndinu wani basi
ZILI BOO
Better
Koma yah luso mulinalo akulu zabwno zose wakhazka nymboy
Mbambande!!!!!!
Mumakwana agiboh eeee km nayiyi nde mwaphatu!!!
Nyimbo zizikhala zopeleka uthenga mumaqana brother
King cha dad umakwana apearson ndinu one bas
Koma Giboh pearson,
basi kumeneko kundikakamila kufunitsitsa ndikale mbali yako?waitha basi.chifukwa nyimbo zako zonse palibe mbola
So good
Ulumu wanu big man
Gibo ?????
Ee km iyi ndiye mwaphatu boss
Am s bee zambia I like your songs
Koma iyii wapha chadadi
Galu ndinu aka mwana mbwàa ????
Zilibwino mbambande
Mbambande
"Njira" ndinu katundu waboma mwaipha nyimboy
Ndaikonda!
Wapha heavy
Iyiyi wapha ase ??
Umatiimirira iweyo
"Galu ndine". Our own local star??✈️