Watch and Download Music Video



Download this video

Vote For This Song

Lyrics

Puputa Misonzi Lyrics Chorus Iwe Puputa misonzi yako/ nthawi yako izakwana/ Iwe puputa misonzi yako/ Ambuye ali nawe cholinga/ Iwe puputa misonzi, Misonzi! MISONZI , misonzi yooo/ Verse1 Ndikudziwa umazifunsa, does God really exist? / is his existence really iust a myth?/ wayesetsa kupempera kwa nthawi yayitali/ panopa ungowona ngati ukutaya nthawi/ aja unkawanena kuti awa ndi otayika/ akunjoya ndi moyo iwe ukungovutika/ ooh U think life is so unfair/ even worse its like nobody cares/ U Cant sleep, ur face covered in tears/ Uli ndi mantha, ur best friend is ur fear/ Kuyesetsa kulimbikira, zinthu osagwira/ Nchifukwa chake mam'mawa umadzuka okwiya/ Koma pali chimodzi chomwe iwe sukudziwa/ chimwemwe chimabwera m'mamawa nde osalira/ Chorus Verse 2 Mavuto omwe timakumana nawo ife tsiku ndi tsiku/ amatikhwimitsa mu nzimu osati nsinkhu/ nde pena mulungu amatha kuzisiya dala/ koma sikuti amakhala abuye atiyiwala/ Anthu omwe unkawadalira anakutaya/ nakutcha bulutu kape, mphawi nde kazivaya/ koma anthu omwewo ndi amene azakutame/ ali sister please tandigayileni money/ Pamenepo iwe utayiphula zikuyenda/ ukuthandiza ana amasiye ndi amatenda/Nde chonde mukamanyoza anzanuwo muzidziwa/ mulungu si jemusi mawa ndi tsiku lina/ Chorus Bridge Mulungu samawona nkhope/ M'mbale wanga usatope/ I know he's got planz for u and and and u and u/

Sharing is cool

You may also like...



Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments
Hits 11978 Plays. | 7911 Downloads.
« Chikondi (feat Sangie) Nkhani Za Ku Malawi Songs Achisale »

Follow Malawi Music on Instagram