Vote For This Song
Lyrics
PONYA MWENDO LYRICS By Piksy INTRO Okay…intro kaye Hmmm mmm hm hm hm hm Koma ndikaponya beat Ndingobwera ndi ma hit Sikuti ndikukweza kamba mu mtengo…..ndeno.. Mhu CHORUS *2 Koma ndikaponya beat (Ponya mwendo) Ndingobwera ndi ma hit (Ponya mwendo) Sikuti ndikukweza Kamba mu mtengo Pali nyimbo palibe ulendo VERSE ONE P . I . K . S. Y – Piksy Ndikudumpha dumpha luso lisabisike Nyengo yasintha koma sindikhala chete Nyimbo sinkhani, ma style ndi plenty They been doin’ bad…I been doin’ good Angoshara mu hood Angosuta ndudu Ali duu ine ndikuponda ponda Mpake pali mau woti makonda makonda Zikuyenda palibe akutsutsa Akudziwa kuyambana ndi Piksy ndi suicide Tchu-tchu-tchu ndikubwera n’zen-zen Position yanga kuichita maintain Thupi langa lili flexible Atsatsuna ena ati ndiri edible Nde, ndimati nkangogwedeza chiuno Piksy, uzibwera bwera kwathu kuno Shaaa! CHORUS *2 VERSE TWO Ngati Third Eye…..Umajaja Chi Piksy changotuluka mu graja Ngati basket ball ndikunjanja Ngakhale ndiri mtsinje ndikufeela ngati Nyanja Fans ikandiwona chimwemwe kudzaza Zoti iwo amandifeela nzomwe ndimayaza Ma vendor, ma soldier ndi ma panza Amakonda nyimbo zomwe ndimamanza Poti ndimakana 2 andipatsa one Ena amanditcha MC wamakani Kuyankhula za ineyo sikusowa nkhani Kaya zachikondi, kaya za chidani Nthawi zina ndimafeela ngati raster Sorry, ndimafuna nnene kuti master Akandiwona mtima kuthawa Inde, amandibeefa akufuna kungotchuka awa CHORUS VERSE THREE Shaaa Fans imandifeela Mu hood ndingochilla Ma haters angolira Kuphika beef mitu yawo sikugwira Sangazikolope nyumba zawo ndizozira Ndimathoka mwa chipongwe Ati tichite njibwa kuti Piksy agonje Poti speaker imanditchula cousin Microphone amanditchula darling Nyimbo zanga ziri super kuchititsa chiwalo chirichonse kudumpha Nyimbo zanga ziri super kuchititsa chiwalo chirichonse kupuma Nyimbo zanga ziri super kuchititsa chiwalo chilichonse kusuntha CHORUS TILL FADE |
Songwriters
Nthumwi PiksySharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
« Unamata | Maso Songs | Zolapisa ft Phyzix, Tay Grin, Young Kay » |