Vote For This Song

Lyrics

HOOK Mwezi uwale eh Ndikumane ndi dona apa Lija ndi kale eh Mfundo zanga ndiponya apa BRIDGE Kapena ndimenye bibida? Mantha ndiye andidinda Ndikumva ngati ndadzimbidwa Pompano nditha kubibidwq VERSE 1 Sikapatali kadonaka nkapatsidyapa She's never heard of me zokuti ndimachita cha She's on point Nkowala ngati dzuwa Nde kamachita kudziwa Koma ulemu wokhawo She is more like an angel She z beautiful and humble Duwa duwa bambo Kukongola kwake kunabwera mma bundle Hmm Mano okhawo ndi malonda a colgate Uyu yekha ndichita zotheka akhale soul mate HOOK Mwezi uwale Ndikumane ndi douner apa Lija ndi kale Mfundo zanga ndiponya apa VERSE 2 Anzanga andiuza zimafunika kufewa Koma ena andiuza nzongofunika kupewa Malangizo onsewa Ndinene mosanama andipangisa kufeela ngati mbewa At some point its true Kukanidwa nkowawa nkamuuziratu zikhale zodziwa anthu two Apo biii.... No i wouldn't hurt her She wdnt hate me I wouldn't let her Chomwe ndufuna ndi chikondi Nothin more Sindziwa za mawa but i know i will be the best man she won't need another Her man and her brother Awesome couple ya pa magazine cover We gonna travel the world i mean every word Anthu adzatitchula love birds Chikondi cha muyaya it will never end NaBola akongolola HOOK Mwezi uwale Ndikumane ndi douner apa Lija ndi kale Mfundo zanga ndiponya apa Chikondi changa nchokoma ulawe Ndimafunitsitsa ntadziwana nawee Ndikakuwona ngati ndithaawe Kukanika kulimba mtima Mutuwu umaima BRIDGE Kapena ndimenye bibida? Mantha ndiye andidinda Ndikumva ngati ndadzimbidwa Pompano nditha kubibidwq HOOK Mwezi uwale Ndikumane ndi douner apa Lija ndi kale Mfundo zanga ndiponya apa

Songwriters

Piksy

Sharing is cool

You may also like...Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Mwezi Uwale is featured on Piksy's upcoming album Mthunzi. The song sees Piksy nervously contemplating how to declare his love to his dream girl.

Comments
Hits 32798 Plays. | 40940 Downloads.
Mthunzi Songs Moto »

Follow Malawi Music on Instagram