Watch and Download Music Video



Download this video

Vote For This Song

Lyrics

KAMENEKA LYRICS - Piksy Produced by FAMOUS VERSE ONE Ku Mulanje tikafikeko Tikakwelere phiri tikatsikenso Ku Likoma tikadziweko Kuti mitima yathu ikalinkenso Mtima wanga sunagundepo Chonchi ukuthamanga ngati mphepo Moyo wanga sunadumpheko Ku mbaliyi moyo wanga sungavutenso Chiri chonse pamwamba Mosabisa number yathu ndi yoyamba Ngini ikufwamba Si ngini ya wamba Ndeno sindikudanda Uwuwu ndi nchere si soda Izi zokha ziribe ma boarder Ndakhala ndikusakasaka Ndeno see zomwe Mbuye wandipatsa... CHORUS Kameneka Kameneka Kanazula mtima wanga Ndi kameneka Kameneka Kamenekaka Kanazula mtima wanga Ndikameneka VERSE 2 Waisokoneza yanga system Iyeyu ndi katakwe ineyo ndi victim Sizingatheke kupanga quit Poti ndiribe choice akusunga yanga nthiti Watenthetsa dziko linali cold Kapena uyuyu ndi ngelo kodi? Akakhala pafupi I'm never bored Chikondi ndi ichi pa iye i thank God Mukafuna ma details Ndiwatumiza pa email Koma among all the females Wabwino ndinasankha ndineyo Mukafuna ma details Ndiwatumiza pa email Koma among all the females Kanga ndi CHORUS Kameneka Kameneka Kanazula mtima wanga Ndi kameneka Kameneka Kamenekaka Kanazula mtima wanga Ndikameneka Kukazizira ndi ka mbaula Umbrella mu Mvula Kosagulika ndi dollar Kameneka kandidaula Kukazizira ndi ka mbaula Umbrella mu Mvula Kosagulika ndi dollar Yeah Kameneka Kameneka Kanazula mtima wanga Ndikameneka Kameneka Kamenekaka Kanazula mtima wanga Ndikameneka hey CHORUS Kameneka Kameneka Kanazula mtima wanga Ndi kameneka Kameneka Kamenekaka Kanazula mtima wanga Ndikameneka

Sharing is cool

You may also like...



Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments
Hits 110893 Plays. | 111268 Downloads.

Follow Malawi Music on Instagram