Vote For This Song

Lyrics

"Kuyambira Lero" Full Lyrics by Kelvin Sings VERSE 1 Ndinafatsa kulingalira ine nkhawa inandigwila ine madandaulo onsewa dziwa amasautsa ntima wanga komwe kuli kokuya si komwe ndinaponya mbedza yanga BRIDGE koma ndazindikila kuti kunja konseku palibe angandikonde ngati iwe kundimvetsa ngati iwe nkona ndidza kwa iwe CHORUS Chikondichi ndi chako chako chako Mtimawu ndi wako wako wako udziwe kuyambila lero udziwe kuyambila zonsezi ndi zako zako zako mtimawu ndi wako wako wako ukamagona usiku wa lero udziwe kuyambila lero VERSE 2 eko ntima wanga utenge palibe wina angausamale bwino chauta nkhawa zathu asenze palibe wina angazichengete bwino nde kulikonse tikafika nyengo zathu zizasintha koma ndiyambe nkupepesa aa pepa dale ndinaswa ntima wako BRIDGE koma ndazindikila kuti kunja konseku palibe angandikonde ngati iwe kundimvetsa ngati iwe nkona ndidza kwa iwe CHORUS Chikondichi ndi chako chako chako Mtimawu ndi wako wako wako udziwe kuyambila lero udziwe kuyambila zonsezi ndi zako zako zako mtimawu ndi wako wako wako ukamagona usiku wa lero udziwe kuyambila lero

Sharing is cool

You may also like...Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments
Hits 14797 Plays. | 39069 Downloads.
« Zonse (Prod. Manifest) Honest EP Songs M.A.N [Mamuna Amene Ndili] (Prod. Manifest) »

Follow Malawi Music on Instagram