Vote For This Song
Lyrics
VERSE1 Kungodzuka mamawa ongodwalika,Ma fever ma headache Zingondiphika, Mimba kuwila mawondowa kufoOka, Apandingomwa Bufen ka pain killer, Kuwona kuti sizikuthekabe, Ma results kubwela ati matenda nje, Ine kuzangoziwilatu,Wakuchipatala ndauyamba akandiyeze, (HOOK) Si malungo,Si zofunika panado, sikusowa kwa magazi, Kapena ma Asazi, Si malungo, Si zofunika panado, sikusowa kwa magazi, Kapena ma Asazi Koma kusowa kwa iwe, kusowa kwa iwe, thupi langa lonseli, kusowa ntendele, Koma kusowa kwa iwe, kusowa kwa iwe, thupi langa lonseli, kusowa ntendele, VERSE2 Nde darling, muzipezeka pezeka,Mukamasowatu ndimangodwalika, Mwina sumadziwa chomwe ulitu Mu moyo wanga kweni kweni nde fasa ndilongosola kah Ndine nyimbo, iweyo ndi Tune oh! Ndiwe chigoli tinakakhala football, Ndine opelewedwa opanda iwe ndichomwe ndikunena baby, heey (HOOK) Mm, maso anga angofuna kukuwonaaHey, Manja anga angofuna kuku ho-daaa, Thupi langa lonseli, likufuna iwe baby, Baby, baabyyy (HOOK) |
Songwriters
BucciSharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments
29759 Plays. | 31265 Downloads.