Vote For This Song

Lyrics

Hook Sindidzakula ine sindidzasintha ine Nthawi zonse kuphaka life Akazi ndimakonda ine ndimawafira ine Nthawi zonse kusaka wife Verse 1 Krazie G Ndina blower!! Easy kaye guys Ndiwonetseni yanga nditi size Ndikapha iyi mundipasa prize Ndimafika pa 21 ndika roller dice Aaah izi Ndinazolowera kupanga Usanditchalenje ndinkazi wako mphwanga Mapeto wake ndimupatsa phaaa Akabwera paden ine ndizamukana Am just chilling by my crib Like it’s just ok and you know what I just made it to day and I told her am CRAZY lil’ something like Jay Z Hook Sindidzakula ine sindidzasintha ine Nthawi zonse kuphaka life Akazi ndimakonda ine ndimawafira ine Nthawi zonse kusaka wife Verse 2 (PQ) Sindidzakula aise Sindidzakula aise Zimene ndikugwetsa pano kuposa mvula ise Olo kulankhula kokha ngati m’busa Olo nkazi wakoyo nditha kugwetsa aise Ukuseka aise Ukuseka aise Ukuyesa ngati ndikucheza aise Tangoyesa aise tangoyesa aise Uzalira pa mawa cha mma 10 aise Wait izi ndizabawa Sindikufuna mpaka zivute pa mawa Koma ndilibe nkhawa Ofcoz ndayaka Hook Sindidzakula ine sindidzasintha ine Nthawi zonse kuphaka life Akazi ndimakonda ine ndimawafira ine Nthawi zonse kusaka wife Verse 3 (Martse) Sindine mamas bwoy Ndine mama star bwoy Ngati ukutsutsa izo nde ndizako Sindidzakula ndili pa Sunday school Ndine mfana wausilu ndili ndi akazi 2 Mukuzimva kukula bwanji mupepere Ngati Varles Kamzere bwanji munyeredwe Umatha ku baker cake nkazi ibekedwe Akunyoza ineyo bwanji asekedwe Anthu akundisaka eya ndili pa market Akazi amandikonda nkhale ndimamwa masachet Martse ofanana ndi masten Nkhani yanyimbo anatenga 10 pa 10 Freshmen!! Hook Sindidzakula ine sindidzasintha ine Nthawi zonse kuphaka life Akazi ndimakonda ine ndimawafira ine Nthawi zonse kusaka wife

Songwriters

PQ, Krazie G, Martse & Janta

Sharing is cool

From the WorldMobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments
Hits 50237 Plays. | 18058 Downloads.

Recently added songs

Details Votes
Fame Zick Fame Zick - Ukudana Nazo
Ukudana Nazo (Hip Hop)
Lim K Lim K - No Money No Life (Prod. Gaffar)
No Money No Life (Reggae)
Yonnexy Yonnexy - Ndi Ambuye ft Young Gibo & Lonte Kay
Ndi Ambuye (Gospel)
Don More Don More - Zipwilikiti ft Twin M & Daima (Prod. Shey Boy)
Zipwilikiti (Afro-Pop)
McLuther McLuther - Gwadapansi (Cover)
Gwadapansi (Gospel)
The Icon Musiq The Icon Musiq - Ndatha Mtunda (Bantaam & Parker Boy Prod. I-Kay GreenLand Rsa)
Ndatha Mtunda (Hip Hop)
Paul Kamwendo Paul Kamwendo - Mama Is Alone ft Madalitso Malula
Mama Is Alone (Local)
Spaitai Spaitai - Mbava ft Hazjey (Prod by JK Warrior)
Mbava (Dancehall)
MRB MRB - Samantha (Logik Mynd Feat Amuna Misso Prod. Misso-Mrb)
Samantha (Dancehall)
B Boi B Boi - Chi Photo (Prod. Ace On The Traq)
Chi Photo (Hip Hop)

Join us on Instagram