Vote For This Song

Lyrics

Tonse tikudziwa kuti Chilima ndi Usi anabadwira momuno, anavepanso momuno, Onse ma bae anagwira konkuno, ndipo akudziwa mavuto a m'dziko muno Njala, nthenda, usiwa, pano zili ponseponse, Ndipo chomwe tikusowa pano ndi nzeru za Mose Atitsogolere tigwirane manja tonse, ndikuyambiranso kutukula dziko lathu lonse Ikakhala sports osachita kutchula, mukudziwa kale kuti mpira amatha kubula Achinyamata aluso tiiphula: ndati achinyamata aluso tiiphula! Hook Mukufuna ntchito tikupatsani Mukufuna business tikupatsani A Malawi voterani UTM A Malawi voterani UTMmmmmm Mukufuna chitukuko tikupatsani Mukufuna chitetezo tikupatsani A Malawi voterani UTM A Malawi voterani UTMmmm 5 years imeneyi taphunzira zambiri, za mmene boma lathuli liliri Through the reforms zonse amadzitsata, koma chomwe chimasowa ndi mpata Chomwe tipange chaka choyamba, kuthetsa katangale, kuchotsa mbava, Kuthetsa quota system, nepotism, presidential powers tidzapanga trim 40 billion anthu a business, boma lilironse: mega farms and factories Tikatero million jobs takwanitsa, apumbwa onse tagwetsa! Hook Mukufuna ntchito tikupatsani Mukufuna business tikupatsani A Malawi voterani UTM A Malawi voterani UTMmmmmm Mukufuna chitukuko tikupatsani Mukufuna chitetezo tikupatsani A Malawi voterani UTM A Malawi voterani UTMmmm Mumafuna kuti apange resign, adziulula za katangale ndani? Akalankhula zinthu zimachitika, kuposa olalikila aja Mani! Palibenso ena angakhonze fast, Chilima ndi Usi ndi nkhenge kumalast Voting UTM, tsono it’s a must, for chitukuko choti chidzapanga last Pa 21 May, vote kapange cast, osalubwalubwa just put us to the test Enawa ndi mafana kachongeni the best, SKC ndi deal, he puts Malawi first Achinyamata, takhulupira, tsogolo lathu lafika! Hook Mukufuna ntchito tikupatsani Mukufuna business tikupatsani A Malawi voterani UTM A Malawi voterani UTMmmmmm Mukufuna chitukuko tikupatsani Mukufuna chitetezo tikupatsani A Malawi voterani UTM A Malawi voterani UTMmmm

Songwriters

Mary Chilima

Sharing is cool

You may also like...Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Tikupatsani is a rap song by Malawi's Second Lady in response to Phyzix's "Mutipatsa?" rap song. The song addresses the key issues raised in Phyzix's politically conscious song regarding the upcoming May 2019 elections.
Comments

From the World

Hits 6279 Plays. | 9987 Downloads.

Recently added songs

Details Votes
Cypher Cypher - Chanco Cypher 2019 [The Comeback]
Chanco Cypher 2019 (Hip Hop)
Ka Sir Blanca  Ka Sir Blanca - Kill Dem Smart (Prod By Alliance Records)
Kill Dem Smart (Dancehall)
Omega XL Omega XL - Osandiuza
Osandiuza (Reggae)
Omega XL Omega XL - Its Friday (Off Your Moods)
It's Friday (Hip Hop)
Nic Thindwa Nic Thindwa - Amayesa Bodza ft Pon G
Amayesa Bodza (Afrobeat)
K Man K Man - Kman - Ima Kaye ft Wakisa James (Prod. Tricky Beatz & Dj Kenlo)
Ima Kaye (Hip Hop)
Deep Harris Deep Harris - 10 pa 10 (Prod By Gonos & Tonicity)
10 pa 10 (Hip Hop)
Frank Waya Frank Waya - Angoni
Angoni (Local)
K-Jee K-Jee - Gold Digger ft IceThird
Gold Digger (Afrobeat)
Eunice Kadzuwa Mhango Eunice Kadzuwa Mhango - Ndapana Iwe
Maloto (RnB)

Follow Malawi Music on Instagram