
SONG
Zabobza ft Gwamba x Phyzix (Prod. Demu Serectah)
Nitrix · feat. Gwamba , Phyzi · Zabodza · Prod. Demu Serectah · Hip Hop
DL 41,845 downloadsST 1 streams
TRACK DETAILS
Song information
MORE FROM THE ARTIST
View artist →More songs by Nitrix
COMMUNITY

Artist
Nitrix ndakutumizila k20 000 ku account yako chake it now
Iyaaa ine nde ndisanameko kkkk
Mmmm Nitrix ndimakani azeru
Damn kkkkk Ana achibwana
Kkkkkk ase iwe ndi tswilu (muchisena) kwabasi kkkkk zoona ine kuthamanga kwa agent kukagula maunits kt ndimvele nyimboy coz pamene ndaona dzina lot gwamba physix ndimati mitchana yakumana apa timva zi
A Nitrix try kuyimbako nyimbo zanzeru nthawi zinazake. Nyimbo zanu fundo ndiye mumakhala mulibiletu malume. If you want to go far with music, yambani kuyimba zanzeru.
Kkkkk umakwana Ada ma3lu bc
????
Hahaha umadziwa, bodza ndi deal.
Kkkkk Koma adha.... Nice one
Kkkk koma Nitrix ndiwe galu ase Hahaha
Kkkkk nice tune
Man mwatilakwira????
Nyimbo yandiponda bho... Ndiya bodza koma ndiya nyatwa heavy,,, ?
Mumakwana ma guy??????
Utibwenzera bundle adhaa ??
Nyimbo mwapha maguy
ℤ????? ?? ?????
matam
Nitrix ndiwe galu???? udyera
Nyimboyi mwaphaaaa
nyc tne
Nyimboyi yilibwino kwambiri heavy
makwana koma.....
Ichi mwapha
Watichapa mutu opanda tsopo ase.
Iwedi ndiwamatama
Ilibho bho
??????