
TRACK DETAILS
Song information
ArtistSkeffa Chimoto
AlbumYesu Ndi Oyela
GenreLocal
Length5:22
File size7.4 MB
FormatMP3
Track1 · Disc 1
Year2025
Added to Malawi Music22 Feb 2025
Downloads17,671
Streams2
Rating4.4 / 5 mics · 22 ratings
MORE FROM THE ARTIST
View artist →More songs by Skeffa Chimoto
COMMUNITY

This song is nice
Thank you for that song Mr chimoto
Excellent
Nice song
yaah jesus ali nic kwambr
Powerf song koma imbilan Mulungu ekha osat andalewa akuchedwetsan
Song ilimwara chief respect to you
Mumakwana big
Good songo mr koma pewewani kukonda ndale
Nyimbo iliyonse ya inuyo ndiyabwino kuphatikiza ndi zimene simunatuluse zomwe
Nice song with good message
Blessed one en my best artist the wh world
Jesus is holy indeed..... powerful song
Inuyoooooo munabwera ndipo kuimba kwanu ndimaitanidwe mulungu apitilize kudalisa tsogolo lanu
Senhor você é meu favorito músico de Malawi, suas músicas me deixa arrepiado e esperança, Deus abençoe você
Skefa unasankhidwa ndi mulungu kuti uzilalikira anthu ambiri kudzera mu maimbidwe keep on brother mmatidalitsa
inu music mumapha za inu sitikaika pa inu mukafika pa taimbani ine kukhosi mbeeee
Ndinazinva nyimbo zako ngt mavumbuluso pepho langa chonde ku ndale kusakuphelen chamoyo muzavulaza gulu timadalisika nanu bwana skeffa
nyimbo ya bwino kwambiri
Iwe NDi katundu aise, umatha kuimba nde ukati ukoke mau eeeh umatha.
You are a blessing to the nation Mr. Skeffa. This song is powerful. Mumatiyimirira
Powerful sound & powerful massage
You were born to sing ?
Iwe ndidolo
Keep it up Mr ??
Inu mulindi madalitso ndipo pitilizani kutidalitsa ndinyimbo zanu bwana
My favorite artist inuyo ndi dalitso nthawi zonse mukamaimba I get inspired
Very nice song from my favourite artist
Great piece
On repeat ??
On repeat ??
Abusa ifetu tathokoza pa ntchito mumagwila mukufalitsa ndithu uthenga tikuyenela kuchita ndikuchitsatila ambuye ndiwa bwino ndi woyela
Zainu timadziwa kale kut munachokela kumwamba kut mudzati pase uthenga wa ambuye mulunguu
Keep the fire burning brother mmatha inuyo tadalitsika ndithu
The living legend
Zamphamvu
I have been waiting for the song, umatha skeffa. Everytime I listen to your songs, I get inspired. Umatilimbikitsa..
Dolo kwambiri ????
Kuimbatu za beserious????????
Very nice song
God is good all the time, achimwene Skeffa Mulungu azikudalitsani nthawi zonse. This song is a blessing
This one is already on repeat here in Zambia ?? ndola to be specific
Sing for Joy?
Nic song my favourite artist
Kakaland boy Ku chalo ,mumatiimira kaka ,ulem wanu
Kakaland boy Ku chalo ,mumatiimira kaka ,ulem wanu
My role model keep it up
Ili BHO nyinboyi