
SONG
Tulani Pansi (Prod. Beat King Kong)
Dan Lu · Tulani Pansi · Prod. Beat King Kong · Afrobeat
DL 66,687 downloadsST 0 streams
TRACK DETAILS
Song information
ArtistDan Lu
AlbumTulani Pansi
GenreAfrobeat
Length3:26
File size5.0 MB
FormatMP3
Track1 · Disc 1
Year2022
Added to Malawi Music23 Mar 2022
Downloads66,687
Streams0
Rating4.0 / 5 mics · 2 ratings
MORE FROM THE ARTIST
View artist →More songs by Dan Lu
COMMUNITY

Atuledi
Ndiwe munthu oowopsa
Achimwene angawa amakwanitsa guys
Wayesesa kamba kakuthi okuva ava komaso sanasiye kuyimba azingopulumusa people in malawi
Nice tune
Nice song
Zonadi atule pansi kupatula zina koma katundu wambili akukwerayo sakuchokela kunja mwachisanzo sugar timapanga tokha pa mchalo pompa dwangwa salima nanga soap komkunonso tikupanga azam nima butex cook
Moto okha okha
Wachiyawo wangalusa.dan lu uli bho osaopa zikutheka apaga
Wayimba chilungamo bro, good work
auze chilungamo Dan atikwana
Osaopa pa chilungamo mapwiya
Mbambande Dan Lu kuyankhula chilungamo osaopa.
Nice song keep up the good work,
Perfect song bro
Mwathoka chilungamo man
He must resign, tatopa ntchito ikhale yoyendera chimanga mmakwalalamu kuononga ndalama zaboma pamene anthu akuvutika
So perfect
Chilungamo
Chilungamo
Apa ndye mwatiyankhulira ngati amava apa ndiye ava
Atulede kape ameneyo
Atulede kape ameneyo
How to study at this university?
Thanks man Dan lu for standing for the Justice God bless you brother (more love)
paja salary inasiya kulowa , ingonenani kuti zathina.....
Sizikugwilizana man nyimboyi ikukamba chilungamo
Atule kumene , chifukwa adanena yekha
Creativity zero in this song,, mukanangolemba kalata uthenga ukanamvekabe
Enter Comment
Mwapha man Dan Lu
Its more than just a song nyimbo ya fuko
Hit song for all Malawians.
Mwatimirira big Dan Lu. Inuyo mwamva kulira kwa a Malawi ndithu
Great song by Dan Lu. Wakwiya ndi mfiti kaoena praise team.
Big up
Ndiwe mbuzi ,,ukulimbana ndi faz yoti si size yako bwanji
Mbuzi ndiiweyo...chomwe unathawira kumalawi kuno kupita ku South ndi Chan mesa mavuto omwewo panopa ndye Ali worse than Mmene unawasiyila muja
Mmm this is beautiful if we had people like u Dan we wouldnt be where we r today
Sizochita kufusa apa mwamasura
Mwaikwapula big. Tulani basi
Bwana mwapha
Bwana mwapha
nice song
More fire bro osawopa
Nyc
Xowonadi ndipo akunenazowona ndipo keep up bro we are proud with you
Mumatha man.
Ilibho
Umayitha boy
Iyi yokha mwandifika pa 1mwina kungovotelathu the song of the year
Chilungamo chimenecho Danlu dziko lawakanika
Mwapha bt man ???
Nailed?
Moo fyah , trakiyi editions
Chilungamo nthawi zina chimabwera ngat mwano big man mwayimba zakukhosi kwanga Ndayikonda nyimbo imeneyi ???
Muli bho ndi2 ma big
Khawawa!!
Since he became a.......... nothing I saw it...
Ur right mr
Nice song bro you are a freedom fight of the nation go ahead to advice our leaders
Nice song bro you are a freedom fight of the nation go ahead to advice our leaders
Nice song bro you are a freedom fight of the nation go ahead to advice our leaders
Nice song bro you are a freedom fight of the nation go ahead to advice our leaders
His message is nonsense
He is the same guy amene amalandila salary ngati lecture koma asali lecture.
Zinthu sizinafike poti Chakwera atule pansi udindo. Honestly things are still under control i
Zoonadi analankhuladi mwina tidikire
Vuto mukakhala simukususa mmapanga convince a malawi kuti tipange mademo koma mukhala mukususa mmakhala zii.. apa muufuna anthu akuthandizeni kutulitsa wina kenaka muzizasusa nokha zaukape zimenezo ti
mi sey weh a on yur side, nuff respek legend ??
Beat ili bho, ndale ndizovuta mawa ndi mkujalino tikuwonani mukumwa Tea limodzi.
Zimangoona kuvuta koma kutula mwaufula kuja mkofunika rather than kut tiontche ma teyala ?
Perfect message
Brother still remember those days kumudzi anthu akamati village champion ha mukutiimilira, en zamveka ngakhale kwa anthu oti ndi agonthi,, Brother u mean a lot mwa Baluku inuyotu nkhani ndiya straigh
Nice hit Dan lu respect to you
Mumakwana biggy?
Ndiye what will change this is the end of days
Kumangwetu ni pesinyasa wetu wamanyi
ndipo akubowaaaa chan
Akungoenela kutula pansi udindo basi tatopa
macv
Wachiyao Wangalusa baba???I support you brother??
Kma iyiyi yokha tikambilane tiigule mofulumila mwachita zomwe ena sanganene mantha atule bass
More fire Don lu awonjeza atule pasidi aaa
Yaku Mombera University zilipati? Kalikonse kakupezani man
Great song%
Wachiyao naga aiweni kut chilambo chikusokonechela wangajogopa kusala chilungamo, kwao kwa chakwera akusekelera izi Dan waimba nyimbo yokuphulan pamoto muyamba usizinamtole Musalimbane naye, mwazimver
Umakwana
Atuled pansi Dada wa
Yele niyisyesyene anene pangali ikwenda apano. Ine ndili pa nyuma penu
Politics ndi game yovuta heavy...
Munali pa salary pano zavuta,
Koma mwamenya heat ya boh
Excellent Dan Lu you make Malawi yo wake up.It seems that some other Malawians are still sleeping
Wachiyawo Wangalusa WW mjomba
Mwayitha man Dan lu nyimboyi kuyiganizila kwambili misozi ikhoza kumangotuluka osalekeza kuganizila malawi pa size yemwe afika awa nde zawakanikilatu atuledi udindo
Iyi yokhayi mwapha bro
Dan lu well said cox apa ndye usogolili sukuyenda bhoo
Atopesa anthu awa eish
Tiyenaye mchewayu athawa yekha osamusiya
Nkhaniyi ndiyoona
Nice song Dan Lu hi 5 form Vaal University
Chulungamo chokha chokha. No harm, attack or offence. Truths told?
Mawu broh apapa wabaya zoona
Wachiyawo wangalusa wakwapula mesa
Zoona
Chilungamo Chinese ngati madz
Atule wakuba watikwana ameneyu
Atuledi ndi mbava ameneyu
That Lil star does. #1 wachiyao
Nice song Dan lu
Mwandifikapo2 apa Mr Dan Lu umakwana bro
Lamula nkon ndinu a Dan lu kuimba nde mmaesesatu
Atuledi ... zawakanika??
atuledi bambo waboza ameneyo watikwana
Awawa zavuta akanangotula
Massive bro keep it up??
Ili nyatwa,zikumuwawa akakolope nyanja?
Chilungamo chokhakha
Umatha 100% massive
Ilibwino
Ili bho man kuwamatsula ationjedza hvy
excellent
Dan lu inuyo umantha ngakaletso Mr nobody
Akuchepha inu ndi number one ulemu wanu
Big Man Dan lu your number one i salute you Wachiyawo Wangalusa bulasa ?✊
Salute my guy
mumakwana munthu wamkulu pomwe yafikadi malawi ayayaya zaojeza akwanilese zomwe analonjeza apo ayi atisiye ndi uphawi wathu omweu asatiojezele kusauka
Mumayitha BG man
Tituleni pansiiii ngt zatinvuta ......tinvele zimeneziiii
Mumakwana
Fact???
Muyawo iyiyi siyamaseweretsa asiye pansi tatopa ndi bwerera zake
Fantastic you the best biggest
Aaaaaaa anyanyadi awa azuzuleni boss eeeeshi mpanje waipa
Best song ever keep it up
Ase hit wapha wachiyawo wangalusa blasa??????✊
Wasowa salary unka landila ija ma mwezi ngati ndiwe ogwira ntchito mu boma kkkkk satula udindo
Mwakwapula malume ulemu wanu
Dan lu umatha Kwambiri. Chakwera atule pansi udindo zankanika
Adzudzulidwe Basi Malawi wayipa?? angokhala ngat siwatonse
Aionjedza, dziko likuwawa ili.
Tikudziws mulu ndi zonse zokuyeneran Home Boi.kma nyimbo mwaimbirs akumuzife..zikono i i think uthenga aumva
Level ya Bho Brasa. Ndipatse Madzi Ndimwere Ndisakomoke mwapha Big Man.
#WachiyaoWangalusaBrasa
Bola Adadi aja eshii
Aaaa tikuzuzika biggy
Atikwezere basic pay ndiye
Nice song. Uthenga aumva. 2025 sipatali ndi pompano akazabwera Ife tidzawathawa. Vote yanga andibwezere. I voted for them just becoz of 1 million jobs pano ati alembana kale.
What an incredible song from Dan Lu with The King Kong. I salute you guys keep it up.
Useless song
Congratulations tula
Nice song big zoona atululedi pansi atikanika Palibe chabwino chilichonse chakwera better malawi uja ali kuti apa
Big up homie ? chilungamo chiyende ngati madzi after vinyo kutha mkuzangoti tulani pansi udindo Mr Habusaaaa
Good
Bola uthenga wapeza kumipandoko ???
Umatha
Relevant song ifeyo ku Zim ndi zomwezo.
Umakwana Dan lu
Umatha iweyo Dan lu, (Notice Mr. Presdent promise is Credit)
Umatha man big up I always check up once you release a new ever
Machine a nyimbo
Not a nice song, but nice and relevant message
This is awesome song wachiya
The song is on point??
Auzeni ankolo,apapa mwachita mowakumbutsa ndithu
Walatsa Dan Lu
Wat a beautiful song thanks my bro matiyimilira
Atule pansi basi, analonjeza yekha zmenezo.
Mumatiimilila brother Dan Luu osaopa kuimba zachilungamo dziko ndilathu ili ufulu anatibwelesela DR Bakili Muluzi
Big up brother, mumatiyimilira,,, you are really a freedom fighter,,,
Wa chiyao......!!!!.... Wangalusa bulasa...
Mwatilankhulila zamuntima big. Moto momo wachiyawo wangalusa
Truth to be told
Zawavuta azibambo avomele
Palibe chanzeru chomwe akuchitadi angotula pansi chinthuchi chawakanika
Zoona zokha zokha dear....some1 has to listen to it and do something shuwaaa
Kkkk APA mwakambatu zoona style bolan asakumangeni
Umafatsa aixe... excellent work.
Fuso langa nali akumava bwanji anthu amenewa akamakhara ndikumatiwona
Atuledi pansi udindo ?
Atule pansi dziko lawakanika ili ?
?
Kwachema
Excellent
Truth hurts.... Wachiyao wangalusa brasa
Moti atsitse sugar, cooking oil ,fertilizer and the rest akukatsitsa bundle for what? Munthu wa kumudzi internet akuyidziwa? Awaganizile anthu akumudzi akuvutika heavy
Wachiyao wangalusa hit song atule
Ine ndiwa Chitonga Wangalusa...... Nyimbo iyi mwapha nsaname... Wachiyawo wangalusa
Zilibwino atule pansi udindo anyapapi amenewa
Awuzeni chilungamo
MMmmmmm paka nyimbo
MMmmmmm paka nyimbo
Nice
Makina
Nice
Mwaphatu big . Big it up
Kwachema ????
Panopa zili worse atule pansi udindo basi