SONG
Ankolo (Prod. Henwood & Tricky Beats)
Dan Lu · Ankolo · Prod. Henwood · Prod. Tricky Beats · Afrobeat
DL 45,913 downloadsST 0 streams
TRACK DETAILS
Song information
MORE FROM THE ARTIST
View artist →More songs by Dan Lu
COMMUNITY

Dan Lu · Ankolo · Prod. Henwood · Prod. Tricky Beats · Afrobeat
Nyimbo imeneyi imandiwadza kwambiri iiiiii!, and ndimayibweledza x100???? mumatha Dan lu

Nice track
Nyimbo imeneyi imandiwadza kwambiri iiiiii!, and ndimayibweledza x100???? mumatha Dan lu
Big up, Nice Tune
angotidyesa ma blue tick aaaaaaaah
Mumakwana BG ankolo liponsepose ndimnambande ine moffat from Lilongwe Elia 49 free mabomba moto kuti buuuuuuu????????
mumantha big zoonadi ankolo bodza kt atenge mpando koma komwe akudyelera
mumantha big zoonadi ankolo bodza kt atenge mpando koma komwe akudyelera
Ili bho heavy
Dan Lu Chilungamo chokha chokha ,zimakoma zili kwa mzako ,lelo ndi izi
Dan Lu Chilungamo chokha chokha ,zimakoma zili kwa mzako ,lelo ndi izi
mhangojonathan52@gmail.com
Za inu timaxiwa kale kwaine mumatiimilira excellent work boss mumangoziwiratu kuti wachiyao wangalusa brother
Bossman Nyimbo mwapha iyi
Good
Ukali wanu ankolo
Ankolo ali Ku mute mesa
Nipapopo ankolo kuchulusa zolonjeza
Made c,siza music izo tangopitan ku school kaye aaah
Made c,siza music izo tangopitan ku school kaye aaah
Iwe galu kwabasi ......osapanga zako bwanji
Nice song ankolo by Dan lu
Wachiyao wangalusa
Nyc one ankolo
Wachiyao wangalusa brasa ankolo mwapha Sound zainu timadziwa uthenga ukuveka bwino kwambili
Ankolo hit iyi ndiye mwaswa koma mtima wanga uli matha panja ena amakulonda ndikare ndiye akava hit iyiyi am sure someone going toiret every one minute
Wachiyawo umakwana ankolo
Iri bho
Nguludi CZ inuyu size dyikana anene,,,, iyiyi mwagazaa
nice song
Excellent BG boss
Ma fill ankolo
Dan Lu super no1 the Malawian bway
Stupid n useless muzik,,,zoba sutha kuimba nyapapi
Wonderful ?
The song is too short...
Nice song bro
Ndimakufirani abwana pa nyimbo zanu simandizutha ngati ndili maiko akunja
Zikutheka
Sound ili bho big up tricky and henwood ntchito munaigwira chabe uthenga unachepa komanso zamilandu
Ndikanadziwa sindikanaomba nemanja,
Wachiyawo wangalusa. Bigup. Akulu. Mwapha
Manyaka
Wapuntha iweyo ndikudikila pa T juga mufika liti
Very nice ???
Nice song(✯ᴗ✯)
Good Song..Tikuvina Ankolo bodza
Mumakwanira big man more fire Ankolo Bodza
Mr Lu nyimbo imeneyi ili bho man!!!!and muli uthenga ? Ankolo on repeat now
Nice song bro
Wow this is super
Yeah zimasithadi , zoona inu mumatha .
oky...nice things ....the instruments are sounding good yah well balanced
Ankolo nyimboyo mwapha ili bho
Super bro Dan
Ili nyatwa ankolo
Ankolo why??
Nice tune ? man dan
Munthu mulala✊✊✊big up my bro
Nyimbo ili nyatwa iyi
Umatha bro nice song
Dan Lu sakhumudwisa ?????
Dan lu ndi more!!!!
Ankolo muli uthenga this song is a great idea
We Stand up with excellent songs
Wachiyao wangalusa ??man Dan lu nyimbo mwapha iyi
Kkk wapambadza Dan mmm
I really like this ????? ankolo mwatiyiwala kuguba konsekuja
The best of the best
Ankolo aaaaa ili boh
Number one song
this is awesome
Sinanga anthu amaganiza kut apindula ndi ankolo awo opanda mpingo hule ofuna kuononga zinthu bas ankolo
Nyimbo yaphedwa iyi ili bo kwabasi
Ankolo Pano Si azanthu
Ulemu wanu wakulu
Good music bro