Vote For This Song

Lyrics

(Verse 1) Hello, Mkaziwanga, I know you know That I love you so.... Ndipolero Ndifuna uziwekut Kubwela kwako mmoyomwanga Wasintha zinthu zambili. Bebi ndiwe Makina ,osokela love yanga.. Daling umaziwa zofooka zamtima mwanga.. Ndipo ndikulumbila I will be with you forever.. My sweet potatoe ....oya ma bebi Oooh. Bebi you are wonderful. I like you body particular. Beb ndiwe umandikweza temperature .. ( I need you to go down , ine sindiilola, mpakanakutopa.) (Chorus) Mkaziwanga iwe iwe iwe...... Ndakukonda ine ine ineyo... Undipase zonse iwe iwe iweyo Mkaziwanga iwe...... (Verse 2) Oyeh ,, oya ma bebi undipase zonse zofunika mchikondi... Pokupanga appreciate nzakupasa tima luwa eeeh... Bebi ndiweyo, Amene , Ine , Ndinakonda ai, ndinakonda ai.. X2 Bebi you are beautiful (elelel mama) I like your body particular Ndiwekha umandikwanila Baby I know that you are feeling me too Let me be the champion in your love Baby. ( Verse 3) Ndiwe... Chiphazuwachanga. Ndiwe.... My one and only ... Unamata mtima wanga. Zilindiwe kut uzandikonde ine... Mwinizithu ndinuyo Mami.. Ndinayamba mwano kamba kainu Mami eeh.. Tiye tikondane iwe ndi ine Mkamakhala mapemphelela iwe..... Mkaziwanga iwe,,iweee ,,,ndakuko ine .. inee... Undipase zonse iwe ,,, Mkaziwanga uweeeee ,,,eeeeh eeeeeeeeeeh...

Songwriters

Thewz G & Kell Kay

Sharing is cool

You may also like...Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments

From the World

Hits 4621 Plays. | 4651 Downloads.