Vote For This Song
Lyrics
| *PEPUSA Lyrics by Phyzix* *(INTRO)* Sameface on the beat {Mphungu Screech sounds} It’s Only Entertainment *(HOOK)* Muwauze kuti mbali zakuno sitipanga nawo za chibwana/ Pepusa Nje! Muwauzitse kuti mbali zakunoko kudelera utupikana/ Pepusa Nje! Kuno timakhafa/ Pepusa Nje! Ndipo tili tougher/ Pepusa Nje! Kuno timakhafa/ Pepusa Nje! Ndipo tili tougher/ Pepusa Nje! *(VERSE 1)* Kundifusa dzina langa ndi kupusa/ alipo yemwe samandidziwa ine Pepusa?/ kundilipilitsa pakhomo ma bouncer/ muuzane kuti imeneyo ndi Pepusa/ Mafana ambiriwa ndi ma Medusa/ makhalidwe ngati njoka akaona khusa/ chomwe amabwelera ndikukuuser ine nde ndine Gangsta sindilora Pepusa/ osandiitana ku show ya dollar yopelewera/ ine ndikafika ku show nde ndimapemelera/ ndine mfana oti ndimakonda kudyelera/ ndimakonda kumwelera ndimadana ndi Pepusa *(HOOK)* Muwauze kuti mbali zakuno sitipanga nawo za chibwana/ Pepusa Nje! Muwauzitse kuti mbali zakunoko kudelera utupikana/ Pepusa Nje! Kuno timakhafa/ Pepusa Nje! Ndipo tili tougher/ Pepusa Nje! Kuno timakhafa/ Pepusa Nje! Ndipo tili tougher/ Pepusa Nje! *(VERSE 2)* Kundiponda sneaker ndekuti timenyanapo/ ngati wamaliza kudya pa tebulo wadyapo/ ine ndine Gamba equivalent El Chapo kumuva mwa u Gangsta zonse tinachitapo/ I demand respect sindifuna za Pepusa/ ndikati ndatchena ngati chimfana cha ku USA/ wina ndikumati za TZ/ Pepusa/ pano ndineneletu ndimadana nzopusa/.. kufuna kudya chimwana ndikudya ndi Pepusa/ kunena kuti Phyzo anatha Pepusa/ ndacharger 10mita wapita ndi 1mita umafuna kundipanga undercut Pepusa *(HOOK)* x2 Muwauze kuti mbali zakuno sitipanga nawo za chibwana/ Pepusa Nje! Muwauzitse kuti mbali zakunoko kudelera utupikana/ Pepusa Nje! Kuno timakhafa/ Pepusa Nje! Ndipo tili tougher/ Pepusa Nje! Kuno timakhafa/ Pepusa Nje! Ndipo tili tougher/ Pepusa Nje! Stich Fray on the board. |
Sharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments
1 Plays. | 9 Downloads.












