Vote For This Song
Lyrics
*NEVER BE ALONE Lyrics by Phyzix, Ruth Kulaisi, Alyssa Grace* Song: *NEVER BE ALONE* Artists: *Phyzix, Ruth Kulaisi, Alyssa Grace* Producers: *Ace Tee Beats, Tricky Beatz, Stich Fray* Label: *It’s Only Entertainment (IOE)* Songwriters: *Noel Chikoleka, Ruth Kulaisi-Chikoleka, Alyssa Grace Chikoleka* Release Date: *August 2025* Genre: *Hip Hop/Soul* *(INTRO: Phyzix, Ruth Kulaisi, Alyssa Grace)* This one for Alyssa (Ace Tee on the beat) Mmmmmmmmh For Alyssa This one for Alyssa You can never be alone Phyzix (My baby) Ruth You can never be alone Captain Bae Mmmmmmmmh Very Good (Very Good) *(VERSE 1: Phyzix)* Ulemu wako mwana wa mkazi/ Ndimadziwa umakumana ndi zambiri (ndi zambiri) Amakuzunza mopanda manyazi/ umapempherabe mbuye awakhululukire (awakhululukire) Unabadwa bwanji kulimba chonchi/ zokupinga ndi zambiri kuposa tsitsi (eh?) Ukuyenera kuziphoda/ sungatuluke pa gate osapesa tsitsi Ukuyenera kudzi holder/ kukanika kupanga zomwe mtima ukufuna Oyenera kukuteteza/ ndi omwe akuyamba kukupweteka (mmh) Oyenera kukukonda/ ndi omwe akuyamba kukugenda (mmmh) Sizingatheke kuti uzakhale wekha/ zokanika munthu amazitha Namalenga *(CHORUS: Ruth Kulaisi, Phyzix)* You can Never be alone/ You can never be alone my baby (x2) Nzosatheka kukhala wekha/ Ingodekha mmmh my baby You can Never be alone You can never be alone my baby *(VERSE 2: Phyzix)* Unabadwa ndi nzeru osaopa kulimbika kuti umposa mwamuna wako (mmh) Unabadwa okongola sikuti unamulola ndekuti aononge nkhope yako (no baby) Usamakanike kugona baby Kuti mawa dzuwa siliwala maybe Usadzasiye kusekelera/ Alipo ambiri okupemphelera (Amen) Oyenera kukuteteza/ ndi omwe akuyamba kukupweteka (my baby) (mmmh) Oyenera kukukonda/ ndi omwe akuyamba kukugenda (my baby) (mmmh) Sizingatheke kuti uzakhale wekha/ zokanika munthu amazitha Namalenga (x2) *(BRIDGE: Ruth Kulaisi)* You can Never be alone. You can never be alone my baby (x4) *(CHORUS: Ruth Kulaisi, Phyzix)* You can Never be alone. You can never be alone my baby (x4) Nzosatheka kukhala wekha/ Ingodekha mmmh my baby (x3) You can Never be alone. You can never be alone my baby *(OUTRO: Alyssa Grace, Ruth Kulaisi)* Nzosatheka kukhala wekha/ Ingodekha mmmh my baby (x3) |
Sharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments
