Vote For This Song

Lyrics

SUDZIWA Lyrics by Phyzix & Quest (INTRO: Quest) {Dziwa} Oh ohhhhh Ace-Tee on the beats {Dziwa} {aaaah aah} {Dziwa} It’s Only Entertainment Oh ohhhhh {Dziwa} Mmhuh (CHORUS: Quest) Kuona maso a nkhono nkudekha {Dekha Dekha Dekha Dekha} Kusamala moyoso nde ndiwekha Kukonda munthu ndi wekha Koma osaiwala kumazikonda wekha Poti chobwela mawa Sudziwa/ sudziwa Sudziwa/ sudziwa Sudziwa/ sudziwa Sudziwa/ sudziwa (VERSE 1: Phyzix) Anali mnzanga koma pano tinadana/ wachikondi wanga uja sitityakhulitsana/ Ena tinadana chifukwa cha mtsikana/ ena kukula mtima basi ku sizer'na/ Zambirimbiri zimatiphinja talking about it brings relief/ zanga ndimaziika munyimbo brother that's my release/ kusaka ndalama but really searching for peace/ wanna make clean money ndisamathawe Police/ ungadziwe tsiku lomaliiza ndi liti?/ awa ndi Akhristu kapena afiti?/ akatisunga kapena amakonda ma skirt?/ banja ndikupilira kapena mpange quit? (CHORUS: Quest) Kuona maso a nkhono nkudekha {Dekha Dekha Dekha Dekha} Kusamala moyoso nde ndiwekha Kukonda munthu ndi wekha Koma osaiwala kumazikonda wekha Poti chobwela mawa Sudziwa/ sudziwa Sudziwa/ sudziwa Sudziwa/ sudziwa Sudziwa/ sudziwa (VERSE 2: Phyzix) Sitimadziwa tsiku lolemera olo losauka/ sitimadziwa kuti tikagona mawa tiuka?/ Kunjaku kukacha tiipeza ya Ufa?/ Kodi ndi chikondi kapena kapena akutiuser?/ Mumazipeza bwanji pamene ife tuzisowa/ sitimatchuka koma nafenso tili ndi malusowa/ kalikonseko m'nakaona mboni ndi masowa/ kalikonseko m'nayesapo osapeza cholowa/ poti za mawa sudziwa sudziwa/ utha kumavala ma suit wa suit wa/ kenako mawa uli ndi usiwa ndi usiwa/ chinyumba chabwino kusanduka siwa/ yeah (CHORUS: Quest) Kuona maso a nkhono nkudekha {Dekha Dekha Dekha Dekha} Kusamala moyoso nde ndiwekha Kukonda munthu ndi wekha Koma osaiwala kumazikonda wekha Poti chobwela mawa Sudziwa/ sudziwa Sudziwa/ sudziwa Sudziwa/ sudziwa Sudziwa/ sudziwa (OUTRO: Phyzix & Quest) {Sudziwa aaaah} Phyzix {Sudziwa aah ah} Quest {Sudziwa aaaah} Yeah {Sudziwa aah ah} Very Good Very Good

Sharing is cool

You may also like...



Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments
Hits 1696 Plays. | 6508 Downloads.

Follow Malawi Music on Instagram