Vote For This Song
Lyrics
Intro Gafar on d board(yah) one 2 wanthu mabilinganya (mabili x5) mabilinganya (mabili) Empire laaaarge!! Nepia dema feel defia! Bridge (Nepman) Aka ndika mfuti Mpaka nakatengera tchuti(mm hu) Ndi love ya muti Ena kudabwa kuti ndi naka tenga kuti(ee he) Hook (Nepman) (Ulingati panado x2 Umandi mvetsa bwino lomwe ndika dwala. Ulingati ndege x2 umandi tengera kutali)x 2. Verse 1 (Jay Jay Cee) baby ulingati jet,kapena helicopter/ Ine patient, ndiwe wanga doctor/ ine passenger ndiwe yanga motorcar/ ine chidakwa ndiwe wanga vodka/ uli fly umanditengera ku jupiter/ pankhondoyi baby ukhala victor/ ngati chinangwa si nsiya kukuta/ nane nalero mpaka thukuta/ Chorus Verse 2 (Tamunyata) ndakondako akazi enawa/ komano ndinawa siya anali ndi chikondi cho burna awa/ ndinapeza iweyo wondi chilitsa/ ndikafoka ndiweyo wondilimbitsa/ umanditengera kutali kuli nyenyezi/ umandi twanima mmaso ndiwe nyenyezi/ ndikakhala ndiwe ndimaona heaven/ Uzandi pangitsa ndikupatse ana eleven/ Bridge (Scola Fella) (eeeh)Ulingat nyimbo za ma Rasi/ ndimafuna ndizingo mvera basi/ iwe ndi waine mpweya/ i can not live with no air/ Chorus Verse 3 (Dotolo) (yoh)tima sarge wez ndikabwera ndita topa/ umandifilitsa nde ndimafila proper/ chikondi sumayeza nd litmus paper/ sulakwisila dala kumandiuza dotolo pepa/ ndili ndi iwe as you wish no compulsory/ umazipereka umayenera uzilandila salary/ yes! I will commit no adultery/ akut ndina gwera makape akut nza lottery/
|
Songwriters
Mabilinganya Empire (Dotolo, Jay Jay Cee, Scola, Tamyata), Nepman, GaffarSharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments

« Zomwe Ndimafuna | Mabilinganya Singles Songs | Mabilinganya (Fake Prophets Riddim) » |