Vote For This Song
Lyrics
ye ye yeee yeeeh oh Yeeeh Tellem aha Yeah here we go Ndimafunitsitsa nditakhala wabwino Aliyense atamatengela ine Ndimafunitsitsa nditakhala chitsanzo Cholozeka pagulu la anthu Koma nthawi zambiri Ndimagwetsedwa Mphwayi Chifukwa Cha zinthu zondizungulila Ndati nthawi zambiri Ndimabwezedwa mbuyo Chifukwa Cha zochita za anthu ena Moyo wanga aha Njira zanga izi Ndimafuna zizikhala za Yehova yekha Thupi langa aha Ntchito zanga izi Ndimafuna ndizichita za Yehova yekha Moyo wanga aha Njira zanga izi Ndimafuna zizikhala za Yehova yekha Thupi langa aha Ntchito zanga izi (Izi) Ndimafuna ndizichita za Yehova yekha Ndimafuna Njira zanga utasintha Ndimafuna Koma zimandikanika Ndimafuna Ndimafuna kukomana Ndimamuna Mamuna wa mtanda koma Koma ndikazamva za abusa Awapezelela ndi sister NKHANI ija ayiphiphilitsa Ine sizimandilimbikitsa ehe Ndikaona zophinja Sindichedwa ine kugiva Sindisilila u beliver Ndimaona ngati ndichedwa ehe Moyo wanga aha Njira zanga izi Ndimafuna zizikhala za Yehova yekha Thupi langa aha Ntchito zanga izi Ndimafuna ndizichita za Yehova yekha Moyo wanga aha Njira zanga izi Ndimafuna zizikhala za Yehova yekha Thupi langa aha Ntchito zanga izi Ndimafuna ndizichita za Yehova yekha Moyo wanga aha Njira zanga izi za Yehova yekha Thupi langa aha Ntchito zanga izi za Yehova yekha Za Yehova yekha za Yehova yekha Zizikhala za Yehova yekha Za Yehova yekha za Yehova yekha Iye Yesu |
Sharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments
