Vote For This Song

Lyrics

INTRO Uu yeah pepani chemwali Pepani adona Chikondi ndilibe Chikondi ndisowa Ndilibe ndilibe ehy! #HOOK Pepani chemwali×2 Pepani adona×2 Chikondi ndilibe Chikondi ndisowa Chikondi ndilibe Chikondi ndisowaaa ah #VS 1 Chikondi kuchi-player Chikondi kuchiyesa Usalire poti wabetsa Usalire pot waliza Chikondi nchotani Mtima ndiotani Ndinali ofatsa odekha ,odekha,izi ndi izi ine ayi Koma leronso mwaliwe Wandifunaso bwanjiwe Ndilibe chikondiwe Ndilibenso mpata owe Chikondi ndilibe Chikondi ndisowa chikondi ndilibe Chikondi ndisowaa #HOOK HOOK HOOK #HOOK HOOK #HOOK Chemwali pepani ndithu Chikondi sima-share U need to take care Komaso kunvetsetsa Nakuuza izi leka Nasamala iwe wekha Nakuuza udzalira Iweyo udzandisowa Chikondi ndinali nacho Pa iwe anga maso Pepani ndilibe kaso Poti mtima waswekaso Chikondi ndilibe Chikondi ndisowa Chikondi ndilibe Chikondi ndisowaa #HOOK HOOK HOOK #HOOK HOOK #HOOK #BRIDGE Uu yeah pepani chemwali Pepani adona Chikondi ndilibe Chikondi ndisowa Ndilibe ndilibe ehy! #HOOK HOOK HOOK #HOOK HOOK #HOOK BAKINGZ;;;inu Inu Sortie Babie Sortie Babie

Sharing is cool

You may also like...Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments

From the World

Hits 1363 Plays. | 712 Downloads.