Vote For This Song
Lyrics
Bebie upitirize Intro: Ndi Alinafe e! Jimu bebie ndikuti upitireze, upitireze kundikonda. VERSE ONE Tachoka kutali iwe, tapanga chibwenzi mokwaniraTazemeberana bebie. Sono lero ndikufuna kuti, Tingomanga oyera, aliyense adziwe. Kuyambira pa chibwezi, sinaone vutto lina lililonse kwaa iwe, Chako chinali chikondi. Koma poti achikondi ambiri, Amayamba bwino chonchi, koma sapitiriza. Ndichifukwa chake ngakhale chikondi sapempha, Ndikupempha upitirize, usalekelere panjira bebie. Bebie! Bebie! Chorus Bebie upitirize x2Upitirize kundikonda. Sweet upitirize, ladie upitirize! Upitirize kundikonda. Bebiee! X2 upitirize kundikonda. VERSE TWO Analiponso wena dzana, anayamba ndichikondi koma sanapitirize.Ambiri amango kondana pachi bwenzi pokha, kumamasukirana kumayenda shosholo, Akakwtirana mumv agawanapo zida. Pamene tikugwirizana dziwa alipo ena, ofuna tidane azitiseka, Chonde usawapatse m’pata. Zomwe nkuchita m’paka mubanja ndzaona chikondi changa Sichidzasintha. Bebie! X2 Chorus |
Songwriters
Alinafe JimuSharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments

« Mabanja Aphweka aka Zinyenyeswa | Time is money (Live Acoustic) Songs | Wamoyo Sayamikidwa ft Duster Namakhwa » |