Vote For This Song
Lyrics
Chorus Akusata kutchipa x3 ee!Mukuzitchipitsa nonkha x2 VERSE ONE Sionse amakufunsila chifukwa chakukongola, ambiriwa akusata kutchipa.Pakuti wena kufunsira kumamwavuta, sono inu m’mangopereka ma cotation. Koma mukuzinyasiraniji?? akazi abwino oyenera pa banja ngati inu. Ine chikundinyas simukuona saizi, mukumavulira tiwana. Akuti wakwatila waluza, akazi amasikwano alibe mwini Akuti kukana amuna ndi ntchimo, koma kumangololla aliyense bola ndalama Komabe CHORUS VERSE TWO Ndiwe mkazi wamtundu wanji? Makani ngati makaniko wa fegi.Uhule omwewu m’paka kuvalira worksuit, Wati unafa kale zako zinada. Lero waitenga ngati profitable business, But you don’t know what will happen tomorrow. Siku lina sundaufunanso, utawonda ngat nthiko ophikira m’memo. Makolo ena okutha mapulani, amatuma ana awo azipanga uhule. Eti kumachita kuwapasa target ngati minibus, Lero ndi izo wabweretsa matenda. Musadabwe!! Chorus VERSE THREE Zoti kuli matenda alibe nazo ntchito, iye kwake ndikudabulisa amuna.Amanena monyada ali asafuna asiye, ati jelasi people never win. Mabanja akale an’kati akafunsirana, chaka chimatha asanalolane. Koma lero ndizapompo pompo kuthana kuthana Akunmango kuudza ndalola koma ndilandiliretu (Ambere chire bola change!). Chorus |
Songwriters
Alinafe JimuSharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments

« Misomali (Live) | Time is money (Live Acoustic) Songs | Mabanja Aphweka aka Zinyenyeswa » |