Vote For This Song

Lyrics

Artist :Ace Jizzy Song :Winiko Prod by :Janta,henwood & Malde Intro ; ndine nfana OGEZA mboni yanga ndi SPONGE// ndine nfana OWALA bestie wanga ndi TORCH// ndimakapewa ti BANana...NTCHOCHI yeah !! (make space for the ace) HOOK ndahasa ndasanja lero ndili BHO !! kwacha yapezeka ndili mma WIN'KO ukauze kamfana kakumwa WIN 'KO kut ndimadana ndi zopusa ine ndi WINIKO Verse 1 mamuna wako ndi zoba monga anzako saku KHAFA ? //akamanga NAMAZAN ndekut siakudya BAFA// iwetu unagwidwa ndi kape alibe BRAINS nkomwe// amayenda wapas alibe BENZ nkomwe// zaine mwayenera kuSIMBA//nditsegula ma SHOP inu mukutsegula MMIMBA//ndili mma WIN'ko ife si aNZANUTU//ndimavera MKAMWA ndimadana ndi zaNKUTU// mfana apa ndiye zako ZADA ZADA //ndati ine si mphwako GWADA GWADA//pali kwacha ndima worker'po HARDER HARDER //ndine king of the jungle DADA DADA//mukaphwekesa tikudulanipo...MAKOSI//tima reader ka life ka simple...MA BOSS//am di maadest tin GIBO...LANTOS// malde beats and Mr Ace jizzle...MATSOTSI HOOK ndahasa ndasanja lero ndili BHO kwacha yapezeka ndili mma WIN'ko ukauze kanfana kamumwa WIN'ko Ndimadana nzopusa ine ndi WINIKO Verse 2 ndine nfana wazaMMUTU ngat DUKU// look ! kutchuka kuposa bengo pa faceBOOK//uku mafana ambiri amandi WELENGA ndine BUKU//ndimakapewa siti panga MATCH...KUKU//simuyakiranji yankheni RASTA ?? //ine ndi JACKIE CHAN drunken MASTER //akhalatu akundiuza padhen kut FATSA//kma ena akandiitanira mmangoti amen PASTOR//sitisonkha MOTO ife timasonkha DOLLAR// BUSH D ndi COACH ife timakonda BHOLA//ahaha MY DEAR NAMBE//unapanga chibwana chogwidwa ndi MBIYA NG'AMBE//mukaphwekesa tikudulanipo... MAKOSI //tima reader ka life ka simple...MA BOSS //am the maadest tin GIBO....LANTOS //Malde beats and Mr Ace jizzle...MATSOTSI Back to chorus Bridge Nfana apa ndiye zako ZADA ZADA //ndati ine simphwako GWADA GWADA //pali kwacha ndima worker po HARDER HARDER //ndine king of the jungle DADA DADA Back to chorus (the last chorus repeats 3

Sharing is cool

You may also like...Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments

From the World

Hits 4685 Plays. | 2090 Downloads.

Follow Malawi Music on Instagram