Watch and Download Music VideoDownload this video

Vote For This Song

Lyrics

Chorus Ndife ana anu Ndife ana anu Msatilore tisauke Ndife ana anu Ndife ana anu Msatilore tivutike Verse 1 Malawi dziko langa lokondeka ah Lomwe ndinalikonda ndili mwana ah Koma zambiri zapotoka Zaloza kuzende Chonde mbuye, unikilaaanipo Chuma chathu ngati dziko mchofooka Anthu ambiri dziko langa ngaumphawi Mene muchilitsa China Mudalitsa America Naye Malawi mumkumbukireee Chorus Ndife ana anu Ndife ana anu Msatilore tisauke Ndife ana anu Ndife ana anu Msatilore tivutike Verse 2 Zotupa zamubongo komaso m`mimba ah Bp cancer komaso sugar ah Imfa za amayi apakati Ana ogwiliridwa, odwala edzi muakhudze ndinuuuu mbuye Sambitsani misewu yathu ndi mwazi wanu mbuye Ngati tachoka amoyo tikafike Dalitsani atsogoleri, amipingo azipani atilamulire Umo mufunila halleluyah Ndikamaliza ntchito yanga, yoimbayi Ndizatseka maso, ambuye adzandiitana Ndiye otsalanu, musazatope, kumpemphelera Malawiii Chorus Ndife ana anu Ndife ana anu Msatilore tisauke Ndife ana anu Ndife ana anu Msatilore tiyaluke Bridge Mbuye malaawii Dziko langa, dziko langa Dalitsani Malaawii Dziko langa, dziko langa Chorus Ndife ana anu Ndife ana anu Msatilore tisauke Ndife ana anu Ndife ana anu Msatiloere tivutike

Sharing is cool

From the WorldMobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments
Hits 44003 Plays. | 35325 Downloads.

Recently added songs

Details Votes
Namwino Chipi Namwino Chipi - Chimkazi Changa (Prod Henz B)
Chimkazi Changa (Local)
Prince 1 Prince 1 - Feeling Crazy (Prod. Ronz Vium Records)
Feeling Crazy (Afro-Pop)
Ballon Ballon - Shingili Gwaragwara (Prod By Tricky Beatz & Terminalz Lab)
Shingili Gwaragwara (Afrobeat)
Wex-Lu Wex-Lu - So Blessed
Sweat Pain and Swagg The Mixtape (Hip Hop)
Wex-Lu Wex-Lu - Respect
Sweat Pain and Swagg The Mixtape (Hip Hop)
Wex-Lu Wex-Lu - Gonna Make It
Sweat Pain and Swagg The Mixtape (Hip Hop)
Wex-Lu Wex-Lu - Ndimakukonda
Sweat Pain and Swagg The Mixtape (Hip Hop)
Wex-Lu Wex-Lu - Memories ft Cyrus & Kay G
Sweat Pain and Swagg The Mixtape (Hip Hop)
Wex-Lu Wex-Lu - Love For My Fans
Sweat Pain and Swagg The Mixtape (Hip Hop)
Wex-Lu Wex-Lu - Ndiyankhule ft PG
Sweat Pain and Swagg The Mixtape (Hip Hop)