Watch and Download Music VideoDownload this video

Vote For This Song

Lyrics

Verse one Anthu ena ndi dzilombo, Ukangoiphula mpamene waputa nkhondo Ayiwala nawo ndi dongo Atamenya hustle nawo angafike pompo Alimbikira kumenya maupo kubindikira kukupempherera down fall Ayiwala mulungu si munthu awa amvabe kuwawa Bridge Asiye athoke Koma nje usafoke Poti adzasintha nkhope Likamukwanira la forty Adzadya matope Zidzatha dzilope Nde adzasintha nkhope Likamukwanira la forty HOOK Forty x3 Limakwana la forty Forty x3 Lidzakwana la forty Verse 2 Akuyuza Facebook Kuwauza anthu ati iwe wa Duu Ati ulibe kanthuuu Kumenya ma comment kumaseka with fools Kumachulutsa ma excuse Sakugwira ntchito angokhalira booze Munthu koma maganizo ngati mbuzi Chifukwa chakeno they still loose Bridge Asiye athoke Koma nje usafoke Poti adzasintha nkhope Likamukwanira la forty Adzadya matope Zidzatha dzilope Nde adzasintha nkhope Likamukwanira la forty Hook Forty x3 Limakwana la forty Forty x3 Lidzakwana la forty

Songwriters

Piksy, BFB

Sharing is cool

From the WorldMobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments
Hits 55689 Plays. | 47145 Downloads.

Recently added songs

Details Votes
Chris Chris - Nkhaza (Prod. by Prosper)
Nkhaza (Reggae)
Yung I Yung I - Sindingapange (Prod. by Prosper & N.O.C Beats)
Sindingapange (Rap)
Izzy Izzy - Moving On
Singles (Afrobeat)
Izzy Izzy - Sukuziwa
Singles (Afrobeat)
TrueChip TrueChip - Olowale (Feat. M'inkliza Mereka)
Olowale (Afro-Pop)
Vistar Vistar - Gwetsa (Feat. Broun Boy)
Singles (Rap)
Taddy Taddy - Kanga
Kanga (Afrobeat)
Grey Man Grey Man - Misozi (Feat. Eustex) (Prod. by Slim K)
Singles (Afrobeat)
Cynik Cynik - Mveka (Feat. Thugger & RapperCenta)
Singles (Rap)
Sky Buzzy Sky Buzzy - Sweet Life
Singles (Rap)

Join us on Instagram