The track is just so good, keep it up brother Azizi. Mumatiyimilira!
C
Cassim
This is one of the most powerful song. content mbambande, arrangement kawawa. iweyo simunthu wamba. i have heard this song pa Ufulu FM and had to search for it. it touched the heart.
D
Don cee
Azizi iweyo umatha aise,,,wish uh more year
M
Mike jnr
A2i2i ? ?
A
Armson ngozo
Iwe ndi machine opangira machine azake
D
Dir Sefra
Yachina A2121 mesa
K
Kerlee Masiva
Koma azizi iweyo umadekha ...thanks Mr story teller ....happy me ndikungoibwereza kuno ku zambia ndikungomva kukoma
J
JACKSY SALANJE BG
Enter Comment A2i2i eee umatha zed khaza pa ript
J
Jutasi
Koma adha inuyo mumatha kwambiri
B
Bonface junior Mahuwela
Azizi you are good in composing songs .nyimbo zako zimandilimbikisa
B
Bambo Aberther
Kumalawi kulimuthu wafundo ndi Azizi
K
Kiga James jay tee
Iyi nde waiphaso koma A2121 kuyimba bwinoku unatengera ndani
D
Dola uyu kwambili big bro keep up
One bro azizi
F
Fedson Leonard
Keep it up,this is nice
S
Syangalosyana
Excellent
I
Ibrahim kagwa
Azizi pa iweyo palibeso umatimvetsa kukoma ndipo umatha
K
Kfra
Umakwana story teller mumativetsa kukoma # A2121 Azizi mit cruzy khanza pa repeat
Y
Yao King GM
Umakwana story teller A2121 iweyo pa mfundo mu music palibe mzako
W
Wizmond nangantani
Koma ndikulumbila azizi nde amandinvesa kukoma amandiyimbila bwino kwambili olo fundo nde zilipo .Mulungu awonjezele nzelu ina .
Enter Comment
Uyuyu ndi katundu
Nkhanzayi muaisua amwene jerasi dhauni...
Good track