
SONG
Mapazi (Prod. Tricky Beats)
Dan Lu · Mapazi · Prod. Tricky Beats · Afro-Pop
DL 43,212 downloadsST 0 streams
TRACK DETAILS
Song information
MORE FROM THE ARTIST
View artist →More songs by Dan Lu
COMMUNITY

Dan Lu · Mapazi · Prod. Tricky Beats · Afro-Pop
It is nice Dan. Keep it up the good work
Nice tune ...inu simunthu wanna?
Mboba mutu sungagwiledi ndlama zapita
Best music
inu zanu timadziwa
Wachiyao jwangalusa ,,, nyimbo yi ilibwino koma kwambili
Umakwana Dada
Mwapha madala
638923
Hit you doin good our boi
Moto kut buuuuuuuuuuuu!
Mwapha man
ZILI bwino kuma last.... anayenda ndi mapazi
Fire brazza wachiyao...
Ulibo upitilize
Nice from ZM??????
Umatha?????
Dan Lu. Ndi nyatwaa!!Enter Comment
Dan lu umakwana
Ili bhob heavy keep it up mr Dan Lu
Mwanza
As good as
This is the greatest song, god continue give you more wisdom
Hey Dan this is a great song.. congratulations brother man
Mwapha sound ngati mwachita kutumidwa big mmakwanila
Wachiyao wangalusadi bulasala
Salute to you big the song is massive
Wachiyawo angalusadi bas
Sound ilinyatwa dan lu, proud of you
I dont know who made or edited or which words can I use moma chikuoopsya chithuzi chake .
Profile ikuonesa uchigawenga gawenga so .
Siyani ndale mani
Ludo lanu ndilachidziwikile that you are t
Zikomo kwambiri panyimboyi
Enter CommentMan dan inu ndinu chipolopolo chaku rasha nice music
Big up Mr Lu lesson is taken.
Dan Lu,, mmmmmmmm bomba after bomba. Akulu mumatha
Dun Lu mumatha kuimba and u have the talent. refrain from politics...its the worse enemy to your career
Iyi mwapha mumakwana D@N Lu
Ulemu wanu big Dan lu
Ulemu wanu Mr Dan lu
Eeeeh apa ndiye Dan Lu wakwapula music akuyenera kulandila ulemu
ili chenene brasa
Ili centene ✔
Mmakwana ma bit anu ndi more
Very fatalistic song anayenda ndi chiphazi
Nice one
Koma tsiku lina tidzanva kuti wayamba Gospel kkkkkk koma ili bho bho
Beautiful track
Good
Painu chipewa ndimavura mumakwana ankolo
Nice track bro
Nice track Mr Lu
Tricky ndi Mwanambwa maningi...
This song munachedwapo amkolo keep it up Mr pesinyasa
This song munachedwapo amkolo keep it up Mr pesinyasa
Nyimbo ili bho mwala mwala
WAWO CHE DANIYELE APATU AWECHETE FUNDO SYAKUONATU
Mumatha
Ili bho tricky saphweketsa ,big up koma Ankolo atikumbukeko kuno
DanLu wabweranso iyiyo ndi Hit ndipo imveka ponse ponse pa chalo chino cha Malawi.
Amkolo mumatiimilira kwambiri ndipo achinyamata ambiri timasangalala tikamamvera nyimbo zanu, Mulungu azikudalitsani pa luso lanu loimba, never give up
Nyimbo wamenya nyatw maka apo ukut satana anaenda ndmapaz safuna tizichita bwno magaye :Dan lu nyimbo zako timaphunzlamo zambiri end umakwana
Ndipo straight
Pesinyasi umakwana
Umatha Dan Lu
Very true, enemies within ourselves, forgetting that tikamakankhirana mmwambwa tonse tizikwela koma tikamakokelana pansi to tigwera limodzi.
Njimbo ili bwino kwambili and ndizoonad tichenjele keep it my Bru pesi njansa
Muli super man. This song will push me on good taking care of wat i hav.
Wachiyawo wangalusa blasa
Matured song.
Umakwanira zatipezeni kuno ku nsanama tizacheze nanu bwana anthu kuno timakufirani hvy