
TRACK DETAILS
Song information
ArtistWikise1992
AlbumKumabweza
GenreAfrobeat
Length4:12
File size5.9 MB
FormatMP3
Track1 · Disc 1
Year2021
Added to Malawi Music1 Mar 2021
Downloads19,697
Streams0
Rating5.0 / 5 mics · 2 ratings
MORE FROM THE ARTIST
View artist →More songs by Wikise1992
COMMUNITY

Amen munthu wa Mulungu.... track ili bho heavy akumaonjedzadi
Nyc song
Amen abusa u have killed the track #Kumabweza ???
Nice track wikise
Ili bwino kwabass
kumabweza
Ili bwino kwambiri
Sitikubweza ngongole abusa
Waimirira 1000%
Ikumveka bho
Ili bho
machine BHABHA Abusaaaa
Ngole zavuta maka ndikolonayu zuvuta or kut umuzindicre wa ngongole wako
Kumabweza ,ilibwino
Nyimbo yirinyatwa abusa Alwz nyimbo zanu muriwuthenga
Mwafwanthamula abusa ulemu wanu
I really like the song..
Yemwe amaimba Chitolilo mu nyimboyi ulemu wake
Abusa ili bho kwambiri respect to you
Koma nyimbo iyiyi mwayikwapula ndithu yili bho ma respect okha okha