SONG

Kalipo (Prod. Steve Meleka)

St Joseph Likuni Anglican Choir · Kalipo · Prod. Steve Meleka · Gospel

DL 1,666 downloadsST 0 streams
↓ Download
Rate this song4.8 mics · 5 ratings
One rating per song per session.
TRACK DETAILS

Song information

AlbumKalipo
GenreGospel
Length6:31
File size9.4 MB
FormatMP3
Track1 · Disc 1
Year2025
Added to Malawi Music11 May 2025
Downloads1,666
Streams0
Rating4.8 / 5 mics · 5 ratings
COMMUNITY

Comments 17

P
Paul Njuli

zamphanvu zamphanvu kwambiri

utumiki paliponse

P
Peter nkhoma

Great song
Ndimangoidusa kom ee yaphedwa kwambiri.. congrats atumiki

C
Crispin Ndhlovu

Anthu mukuimba.
Congrats guys.

B
Blessingchithumba@gmail.com

Nyimbo yabwino

B
Bornface Banda

First time kudziwa group ili koma ndizamphanvu kwambiri . Ambuye azilemekezeka

G
Getrude Machirika

Anyamata amaimba bwino awa, iyinso yandikomera ndithu.

B
Born face Jumbe

Ziribwino ndithu. Uthenga wamphamvu

J
Janet Liphava

Yandikomera nsaname.
Koma ndiye kalipodi.

M
Michael Somba

Nyimboyi yaphikidwa, olemba nkhaniyo anapitiriza pa nyimbo ya Dala ija eti? Muli bhoo guys, keep it up. Uthenga wamphamvu, wosamvayo kalipodi. Producer uyuyu ntchito amaidziwa, ndamtayira kamtengo.

M
Martha Mpachika

Eeeh nyimbo yabwino iyi. Ndaikonda

M
Miracle Baisa

Uthenga wokoma

M
Martin Andrew Nkhoma

The song, Kalipo, is so nice. Keep up the good job.

M
MIRRIAM JIYA

Powerful song

L
Linly Moyo

Eeh yandisangalasa kwambiri

E
Ernest Mpunga

This is a powerful song with strong message
Kudos to u guys

B
Ben Saidi

Very powerful song, uthenga tikuumvadi tsiku ndi tsiku, kusalapaku kalipodi

S
Stain Ley

wow

Kuimba kwabwino komanso uthenga wamphanvu. Ambuye azikudalitsani

Join the conversation

Choose a songmalawi-music.com
0:000:00
🔊