Vote For This Song

Lyrics

Intro Nesnes.., Yeah... Verse 1 Yesu ndimudziwa ine samalephera Yesu ndimudziwa ine amagonjesa Master Jesus there is no one like you Master Jesus palibe ofana naye Doctor Jesus palibe mthenda yomukanika Papa Jesus amakonda ana ake onse Nthawi yamavuto tamuyitane Nthawi yamavuto call his name Chorus Pukuta misozi yako bwelesa Vuto lako Kwa Yesu anali yakho (iyeyo) Alinayo yakho oh oh(iyeyo) Salephera Salephera aaah Salephera Yesu salephera Verse 2 Uvutikilanji nyumba mwa bambo Ako muli chuma ona walemedwa Bwela kwa Bambo ako zakutula Khulupilila iye siliva ndi golide zake Ananesa iye muthawi yamavuto Timuyitane Chorus Pukuta misozi yako bwelesa Vuto lako Kwa Yesu anali yakho (iyeyo) Alinayo yakho oh oh(iyeyo) Salephera Salephera aaah Salephera Yesu salephera Bridge Master Jesus yeah Doctor Jesus kuchikweza Chorus X2 Master Jesus Mfumu Jesus Master Jesus Doctor Jesus X2 Zonse Jesus yeah

Songwriters

Nesnes

Sharing is cool

You may also like...Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments
Hits 9236 Plays. | 8805 Downloads.

Follow Malawi Music on Instagram