Vote For This Song

Lyrics

[INTRO] It’s a king Wa Malawi oohyeah..!! / Mr Ayaya..!!! (Verse 1) Ukamwetulira mtimawu / Dhu-Dhu kugunda / Ukasekelera nthupili / Paliponse kukoma / You look so credible / You the one I love / Para nakusowa vikwenda yayi / Darling ndiwe moyo wa ine / Ukatalikira ndi madwala / Nkhukupenjanga mazuwa yonse / Mawazo ikundivuta / Ndakumising’a masiku onse / Ndiwe provider / Ndiwe chitetezo cha ine / Undipatse mpata / Ndikukonde mpaka mapeto / [HOOK] Tenga zanga zonse basi …!!! Pa iwe ine ndathera Ndiwe nthiti yanga basi …!!! Pa iwe ine ndafika Umandikonderamo …!!! Usamasowe – usamasowe Umandikonderamo …!!! Usamasowe – usamasowe (Verse 2) Ungasowanga yaye / Ishi na mimi / Uwenge nane / Niwewe pekee / Ndimafuna love ya kanthinthi / Yosawona nyengo / Undisambizye mwantinti / Mopanda zilango / [HOOK] Tenga zanga zonse basi…!!! Pa iwe ine ndathera Ndiwe nthiti yanga basi…!!! Pa iwe ine ndafika Umandikonderamo…!!! Usamasowe – usamasowe Umandikonderamo…!!! Usamasowe – usamasowe (Verse 3) Zomwe ine ndinkakhumba / Ndazipeza zili mwa iwe / Aka ndi kanga kanga / Palibeso oposa iwe / Zafika ndikuthangatire babe / Bwera kuno ndikunyadire / Zikavuta usandilalatire hunie / Mwachikondi undilakhule / Wewe ni mwanga / Katika maisha yangu / Ninakuhitaji kila siku / Wewe ni moyo wangu / Unanipa furaha hata / Ukiwa mbali / Kulikonse tingapite apa / Tili awiri / [HOOK] Tenga zanga zonse basi…!!! Pa iwe ine ndathera Ndiwe nthiti yanga basi…!!! Pa iwe ine ndafika Umandikonderamo…!!! Usamasowe – usamasowe Umandikonderamo…!!! Usamasowe – usamasowe [HOOK] Tenga zanga zonse basi…!!! Pa iwe ine ndathera Ndiwe nthiti yanga basi…!!! Pa iwe ine ndafika Umandikonderamo…!!! Usamasowe – usamasowe Umandikonderamo…!!! Usamasowe – usamasowe

Sharing is cool

You may also like...Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments
Hits 278 Plays. | 465 Downloads.

Follow Malawi Music on Instagram