Vote For This Song
Lyrics
Sindidzaku khumudwitsa ayi (Ndiwe Wanga Iwe) Ine ndidzakukonda iwe Ngakhale wina andinene ndiwe ndasankha Kulikonse ndidzapite nawe udzanka Namalenga pemphelo lijano wayankha Mkazi ndiwe wanga, nena inde Sindzaku khumudwitsa ayi (ndiwe wanga iwe) Mkazi ndidza kukonda iwe Monga madzi ozizira Kum'mero kwa yemwe ali ndi ludzu Iwetu ndimaku dalila Ndiwe Koloboli ndine chikhudzu Apasula mamvera-mvera Wachitatu njoka muudzu Mkazi ndidzakusamalira Kukutonthoza ukamalira Verse 2 Ndikufuna kukhala nawe muchikondi Ndiku khulupira ukumva siiwe gonthi Mkazi ndikufuna tidzipanga chonchi Wachitatu ndiwosokoneza moti Momwe ulilimu sindingamenye ndichikoti Ayi, olo khofi indedi mpaka mdothi Ndidzakupatsa chikondi udzati abuna ali ndi muti Ndikakoti zwee! udziti abuna ali kuti Chikondi cha daily, ayi chopanda tchuti Monga msilikali, tsiku lonse kubeleka mfuti Unifolomu ya chikondi, kumapaziku bhuti Ndipamene iwe udzazindikile zoti |
Songwriters
Komuniq Kyrillos, TrumelSharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Komuniq drops another gem from his upcoming Wolakika Reggae album. A love song on a drop riddim provided by Trumel.
« Usalire | Wolakika Songs | Mpando Wachifumu » |