Vote For This Song
Lyrics
Intro Mmh Current situation.. Yeah man.. you Blakjak Indee.... you Desert Eagle, Sispence Akazi Akufuna Dr. Che Whaaaaayahsayyy Indee... Chorus Ati.. Ati Sakufeela bho Akumva fever Komanso Malungo Nde Akufuna Dr. Che Am'baye Dr. Che Am'baye x2 Verse One (Eyoh Eagle) Anabwera Kwathu dzulo Kufikila kulowa Ndili mtulo Kenako Nkudzakoka Ka Pillow Mmnh, Basi pompo tulo Mmwawa Podzuka Akukhetsa msonzi Zatheka Bwanji kuti zifike Chonchi Thupi latenthelatu ngati Patient Oooh God! Latentha ngati patient Verse Two Ati Wadwala Akufuna achile Wakhalira Kugona Akufuna Ayime Adye zipatso komanso Avine Mwezi uwale tisewere Tiimbee Komatuuuu,, Siine doctor poti Nkakubaya poyipa sulira Moti Ati Nzabhobho Kuyankha Mwakhonfii Mmmmm Akuchita Kuyankha Mwakhonfii Verse Three Panopa Nkhani yashupha Ndikungoyenda modumphadumpha Ndinamm'baya nde Watupa Angotulukanso Thukuta Apa nditani Ase Akazi Onse angofuna Dr. Che Komatu Ine ndilibe licence Nditha ndine Nzanu Sispence Chorus Outro |
Songwriters
Blakjak, Desert Eagle & SispenceSharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments
26152 Plays. | 10154 Downloads.