Watch and Download Music Video



Download this video

Vote For This Song

Lyrics

Mdyelekezi M ngotuzuka M ngotuzuka mngotutuzuka, mdyelekezi M ngotuzuka atuzuzuka kwambiri akawona ine!!!! mdyelekezi atuzuka kaona Ine ,alekelenji utuzuka kaona Ine?akamagenda mumtengo muli kanthu.chifukwa chake atuzuka akawona ine*2 Koma mbuye walonjeza kumenyera nkhondo Ine ngati mordecai pamaso pa Harman yo!mlungu wanga walonjeza kumenyera nkhondo Ine ngati David pamaso pa goliaght yeah. chorus mdyelekezi M ngotuzuka M ngotuzuka M ngotuzuka. mdyelekezi M ngotuzuka atuzuka kwambiri akawona ine!! amandiona ndili ndi yes ineyo,amanditutumuka mchifukwa chake atuzuzuka akawona ine. verse 2 adani anga atuzuka akawona ine, alekelenji utuzuka akawona ine?akamaloza mumtengo muli kanthu mchifukwa chake andiloza akawona ine*2 Koma mbuye walonjeza kumenyera nkhondo ine ngati yehosofati pamaso pa a amon wool! mbuye wanga walonjeza kumenyera nkhondo ine ngati ayisilayeli pamaso pa iguputo M mmm back to chorus. verse 3 adani Ako atuzuka akawona,alekelenji utuzuka akawona iwe?akamagenda mumtengo muli kanthu mchifukwa chake atuzuzuka akawona iwe*2 Koma mbuye akulonjeza adzakumenyera nkhondo ngati Daniel mumdzenje lamikango.mbuye wako akulonjeza adzakumenyera nkhondo ngati achina misheck mung'anjo yamotoyo!! chorus fading

Songwriters

Born Kavala Banda

Sharing is cool

You may also like...



Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments
Hits 18528 Plays. | 7066 Downloads.

Follow Malawi Music on Instagram