Vote For This Song

Lyrics

( Intro) its a love song... its ur gal Queen mishuuu its a love.. ( Verse 1) *Hello Bebie tabwela ndikuone eyaaaa *ndikakhala osakuona sindinva bwino owuwoo *chikondi chimenechi sichanormal *mkakusowa ndimafila abnormal *unapukuta misozi yangaa *pano zoliraliralira normal.. *usadzafe udzangosowa eee umandinvesa kukomaa.... (Hook) Usadzafee bae....Udzangosowaaaa Chikondi chako,,chimandinvesa kukomaaa Usadzafe bae,...unabwelesa chimwemwe mmoyo mwanga.. Usadzafe bae, love yako imandinvesa kukomaaaaa.. (Verse 2) *Am so lucky to have you..your one in a million. *Am inlove am inlove with you love yako imaposa billion.. *Ndikakhala osanvako mawu ako *Tsiku langa limabhowaa.. *Ndinathela paiwe honey usadzafe udzangosowa. *Ndikulonjeza sinzakuthawa,,,ndikulonjeza sinzakusiyaaaa.... (Hook) Usadzafee bae....Udzangosowaaaa Chikondi chako,,chimandinvesa kukomaaa Usadzafe bae,...unabwelesa chimwemwe mmoyo mwanga.. Usadzafe bae, love yako imandinvesa kukomaaaaa.. (bridge) Ooooooowa owowo owowooooo Usadzafe udzangosoooooowa Bebie Ooooooowa owowo owowooooo Usadzafe udzangosoooooowa Bebie Usadzafe udzangosoooooowaa Bebie (Hook) Usadzafee bae....Udzangosowaaaa Chikondi chako,,chimandinvesa kukomaaa Usadzafe bae,...unabwelesa chimwemwe mmoyo mwanga.. Usadzafe bae, love yako imandinvesa kukomaaaaa..×2

Songwriters

Queen Mishu

Sharing is cool

You may also like...Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments
Hits 8143 Plays. | 10995 Downloads.

Recently added songs

Details Votes
Bee Jay Bee Jay - Madoo
Madoo (Rap)
GK The Covenant Son GK The Covenant Son - Still God (Prod. Mponya Records)
Still God (Gospel)
Papa Pee Papa Pee - Mundikhululukile
Mundikhulukile (Reggae)
Innocent Chitimbe Innocent Chitimbe - Ndinu
Ndinu (Local)
Innocent Chitimbe Innocent Chitimbe - Zokamba Kamba
Zokamba Kamba (Local)
Zoe Zoe - Amazing Grace
Amazing Grace (Afro-Gospel)
Innocent Chitimbe Innocent Chitimbe - Zanga Zonse
Zanga Zonse (Local)
Shekinah Shekinah - No One Else
No One Else (Gospel)
Lenny K Lenny K - Think About You (Prod. Madela)
Think About You (Gospel)
C Kelvin C Kelvin - Sachedwa Safulumila (Prod. Ace Tee & Dj Brown)
Sachedwa Safulumila (Hip-Hop Gospel)

Follow Malawi Music on Instagram