Vote For This Song

Lyrics

Intro Mmmh mmmh mmmmh mmmmh Che Wikise Baba!! Wakumana ndi munthu wa ambuye.... Nah Nah Nah Nah Nahyi! Stah stah Stah Stah Stahtahyi!! Jungle Jex You Know... Verse 1 Wakumana ndi anyani ambiri, ena ongofuna chipatso chapakati// Osewo amuna ausilu,amkakuona kodi kutchipa pati// Panopa ndi man of God// Omanya kuchenja mastyle// Kuchezakuchezakucheza kenako kumenya masalimo// Mbiri ndainva kumene ukuchoka// Unangogiver ukuku ndikutopa// Mbiri ndainva ndabwera ndifufute// Chikondi chako usati uchifutse// Hook Lero ndi lero ndi lero Chikondi chija uchinveno kukoma// Lero ndi lero ndi lero Chikondi chija uchinveno kusintha// Wakumana ndi munthu wa Mulungu. Chikondi chija uchinveno kukokoma// Wakumana ndi munthu wa Ambuye Chikondi chija uchinveno kusintha// Verse 2 Osakhala ndi mtima odhauta// Wakutengayu ndi munthu wachautu// Ndipo iweyotu uli monyawuda// Ndiwe ogwidwa udziyankha mwa louder// Chikondi changa changa ndichodalitsika// Wakumwambayo kale adachitsilika// Kusintha kusintha kwadzano// Ngati kunali m'dima pano titi kwachano// Mbiri ndainva wafika pongotopatopa// Ndi chikondi chamadobadoba// Sindikukana wafika pongofookafooka// Ndi chikondi chamafoshafosha// Verse 3 Wikise Beib i can see Unakondedwapo ndi achina yudasi Ankangokuzuza dairy kukhalira mambazi But Dont worry Mavuto ako onse atha Ndine wako mesiya Muyaya sinzakusiya Bwera uchilawe chamkachisi Cha abusa chikondi Chama libakateliya malipapakakatala

Sharing is cool

You may also like...Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments

From the World

Hits 11428 Plays. | 13339 Downloads.