Vote For This Song

Lyrics

(SOCIAL MEDIA Song lyrics) HOOK Me wanna talk pon de smart phone(aaah umangodziwilatu) Ku tchesa ma bebie ma friendships facebook watsapp Social media Social media xul bouy Church gal waluza attention Mdala kuchedwa kujob Stern ndowo kupyelela kamba ka Social media VERSE 1 DALA NDIMBOLA Mastern Mastern tipatsenikoni ka dolla Sindikamwera sindikangula mabolla Ndingule phone nane ndiloge Timachick tapa ap nafeso tifuna tiloge Olo kakhale ka china bola media yitheke Marude ma chick ndikufuna muthweke Olo kakhale ka china bola media yitheke Marude ma chick ndikufuna muthweke VERSE 2 Ndine chifana chopsumpha paden ndimamenya Ndimamenya hustle ndipeze dolla yacredt Ndimavutitsa mastern kusowetsa dolla yatomato or ya salt Ndine admir watima group apaposte Wothoka za shirt kuinbox ndimu broke Ngati suli pa whatsapp FB ndekuti sulimu fasho Ndikuuza pa social media ngati ndili ndishow Osandikhola ngati ukufuna kutchila tiye pompho pasocial media Kungwila kankazi kabo achina Joy,Linda,Lidiya Apa ndimenye chindekha ndiposte pa FB Acommente ma nigga ma badman mababy

Sharing is cool

You may also like...Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments

From the World

Hits 3422 Plays. | 1021 Downloads.
« Khala Mphe (Chavura Diss) Singles Songs

Follow Malawi Music on Instagram