Vote For This Song

Lyrics

STICH FRAY Anthu ambiri amakuseka Ndidziwa mtima wako umapweteka Anthu akwanu amakunena Ndidziwa azimzako ambiri amakunyoza iwe Zambiri umazimva, zoona umazimvazo Koma ndine munthu am not perfect ndimalakwaso Mbiri yanga angayidese bwanji u'll always be my baby Well listeni mi nah care wah dem seh coz am down for you baby. Chorus..... Ngat simunayimvele kayipezeni pa Malawi music ilimbweeeee guyz...

Sharing is cool

You may also like...Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments
Hits 25119 Plays. | 23722 Downloads.

Join us on Instagram

LIKE MALAWI-MUSIC ON FACEBOOK

FOLLOW MALAWI-MUSIC ON TWITTER