Watch and Download Music VideoDownload this video

Vote For This Song

Lyrics

Verse 1: Timano tako ukamasekelera Timau tako ukamandiyandkhula Timaso tako ukandiyang'ana,, ndimafa head Timiyendo tako ukaponya step Kambina kako mkumagwedezera Timanja tako tikandikhudza ndimadzifunsa aah.. kuti,,, Pre chorus; Sudzandidyera chuma changa iwe Delilah Sudzawazunza abale anga iwe Delilah Mkundipereka kwa adani Ngati Delilah..*2 Chorus;; Delilah ah ah aaah Unene eeh eh Delilah ah ah aaah Unene eh eh Delilah eeh eh Unene eh eh Ndidziwe Delilah *2 Verse 2 Mwina umphawi wanga siudzatha chifukwa cha iwe Abale ndi amzanga mkudzadana chifukwa cha iwe Mwina udzandiika pampeni, kwa adani anga nena zeni zeni Iwe, siwe woyendayenda ngati enawa/ Sudzanditengera matenda mkundithawa ine Ndimapemphera// kodi mkubwera kwako simdzasochera ine? Mbuye adandidalitsa kodi mkubwera kwako sanditembelera ine? ndidziwe, kapena mwina ntchito mkudzatha Kapena mwina mdzayamba ine kupita... kumanda mtakusiya ndi ana, unene kodi udzawasamala. BACK TO THE PRE CHORUS BACK TO THE MAIN CHORUS Bridge ;; Delilah ah, simfuna kudzalira aah Ngati Samson,ngati samson I say Delilah Sindikukaikila aaah koma ngati samson, simfuna kudzalira aaaah

Sharing is cool

From the WorldMobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments
Hits 140291 Plays. | 90855 Downloads.

Recently added songs

Details Votes
Jah Zeal Jah Zeal - Koma Why (Prod. by Sun Jay)
Koma Why (Dancehall)
X-Tee X-Tee - Amanda (Prod. by Kidy Beats & Dj Sley)
Amanda (Dancehall)
Joe Santiago Joe Santiago - Albino
Albino (Rap)
Wiz Mah Wiz Mah - Monica
Monica (Afro-Pop)
Gun Maddah Gun Maddah - Aweh U Deah (Prod By D-Plo Media)
Singles (Dancehall)
Gun Maddah Gun Maddah - Who am I (Prod By P V Records)
Singles (Dancehall)
Joseph Chiwayula Joseph Chiwayula - Collaborations 2019
Collaborations 2019 (Reggae)
Joseph Chiwayula Joseph Chiwayula - Pakhale khale
Collaborations 2019 (Reggae)
Joseph Chiwayula Joseph Chiwayula - Ndiyimbe Nawo
Collaborations 2019 (Reggae)
Joseph Chiwayula Joseph Chiwayula - Ndipempha M'dalitso
Collaborations 2019 (Reggae)