Watch and Download Music VideoDownload this video

Vote For This Song

Lyrics

Intro: We here Ine eeh, ah ah Ine eeh, ah ah Maluzi ziii, (musiye mzako) ah ah Maluzi ziii, (musiye mzako) ah ah Verse one: (Saint) Munthu wandalama kuitana okukonda ambiri Mpaka dollar akudyere kenako akuipitsire mbiri Nde maluzi akapweteka Amzako onse chekacheka Abaleso sapezeka Pakamwa pawo adacheteka Ukatha ma plan Ngati udye makatani Maluzi ndi chipani Choyambitsa udani Ineee. Chorus: Aah Ine ine yah Ndatchekela Maluzi ndalephela (ah) Aah ine ine yah Ndatchekela maluzi ndalephela (ah ah) Ndangosanduka wolira Ndatchekela maluzi ndalephela (ah ah) Ndatchekela maluzi ndalephela (ah ah) Ndangosanduka okanda Ndatchekela maluzi ndalephela (ah ah) Eeh ndalephela Vers 2 (Macelba) We here Kuyesesa kusaka ndalama Titole chikwama titule minyama Kuyesesa kuthesa ulova poti zikamavuta palibe akutchova Kuthamangathamanga daily Koma mavuto angochuluka daily Mpaka pa line angondikamba Ndichite bwanji kuti ndipeze mpamba Wangongole afuna zake Mkazi wapakira zake ati apita kwa make Mwina ndiyese mtera kapena ndilowe kuba Kukhesa thukuta koma maluzi sakumva ine BACK TO CHORUS Bridge: (Macelba) Musiye mzako ×8 (Saint) mmmh ine eh eh Maluzi ah ah Ine.. mayo mayo. BACK TO CHORUS. Outro (Saint) Ndalephela, ndalephela aaah ah ah ×4

Sharing is cool

From the WorldMobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments
Hits 92394 Plays. | 61898 Downloads.

Recently added songs

Details Votes
Paxton Paxton - Love Is Blind [Paxton & Katelele Ching'oma]
Love Is Blind (Local)
Paxton Paxton - Mwatenga Nsambi [Paxton & Katelele Ching'oma]
Mwatenga Nsambi (Local)
Theo Thomson Theo Thomson - Can We
Can We (RnB)
Madela Madela - Sindisowa Kanthu ft Paul Duncan (Prod. Madela)
Sindisowa Kanthu (Gospel)
Presento Sky Presento Sky - Wachikondi ft Sir Patricks & Gaffar
Wachikondi (Afrobeat)
Wiz Boy Wiz Boy - Usandipatse Busy [Dope Squad Music] (Prod. Kaning'ina Studio)
Usandipatse Busy (Afrobeat)
Squizy Squizy - Dweet ft Ka Sir Blanca (Prod. Blista)
Dweet (Dancehall)
Classick Classick - Intro (Not For Too Long)
Intro (Not For Too Long) (Hip Hop)
Roxy I Roxy I - I Love You
I Love You (RnB)
Roxy I Roxy I - Nsanje (Prod. Khizzy)
Nsanje (RnB)