Watch and Download Music VideoDownload this video

Vote For This Song

Lyrics

Verse 1 (Gule wamkulu)
Msati mseke akadzola matope pepepe pepepe
Atavala chigoba choseketsa kunkhope pepepe pepepe
Amathamangitsa mpaka wina atope pepepe pepepe
Nkumukwapula mpaka wina atope pepepe pepepe
Ndalama yake awafupe pepepe pepepe
Amasamba kudambo osati pampope pepepe pepepe
Amati iwo nvilombo nvilombo nvilombo nvilombo
Napepepe

Chorus
Koma onsewo baibulo liti awafuna
Awafuna a-a awafuna
Eee awafuna a-a awafuna
Abwele avinile iyeyo awafuna
a-a-a-a-a-a-a-a-a
Koma onsewa Baibulo liti awaitana
Awaita-ana awayitana
Awaita-ana awayitana
Abwele avinile iyeyo
Awaita-a-a-a-a-a-a-a-a-na

Verse 2 (Beni)
Msati mdabwe mkaona asilikali lili lililili
Atavala zawo koma zaasilikali lili lililili
Nsapato zawo atapolisha phuli phuli lililili
Akuvina monyada koma cham’mbali mbali lili lililili
Matupi awo atayaka ngati moto kubuka ngati moto kubuka Lhiiiiii!! Lililili
Pang’ono pang’ono dansi nkumakolela ngati ndi mlili lili
Sangavine yekha amavina kagulu ambili lilili

Chorus

Verse 3 (Malipenga)
Msati mdabwe mkaona atchenetsetsa tsatsa tsatsatsatsa
Kabudula ndimalaya zoyeletsetsa tsatsa tsatsatsatsatsa
Stonkeni kampango koyeletsetsa tsa tsatsa tsatsatsatsa
Amavina monyang’wa koma monyang’witsitsa tsatsa tsatsatsatsa
Amamwetulila ngati akujambulitsa tsatsa tsatsatsatsa
eee sungati ubele olo utayang’anitsitsa tsatsatsatsa
Koma sungati uvine olo atakuphuzintsa tsatsatsatsa
Koma Yehova baibulo lati mtifuna
Mtifuna a-a mtifuna
Ee mtifuna a-a mtifuna a
Tibwele tivinile inuyo
Mtifuna aaaaaa mmm mm
Ati koma inu yesu baibulo lati mtikonda
ee mtikonda a-a mtikonda
eee mtikonda mmm mtikonda

Songwriters

Patience Namadingo

Sharing is cool

You may also like...Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Msati Mseke is Patiences first single release in 2015.
Comments
Hits 86815 Plays. | 60256 Downloads.

Join us on Instagram

LIKE MALAWI-MUSIC ON FACEBOOK

FOLLOW MALAWI-MUSIC ON TWITTER