Vote For This Song

Lyrics

1st Verse

Amakhala muchi nyumba cho dula
Panjapo ayimika zima galimoto
Wana akhupunzira ku Bishop McKenzie
Makolo adawagulira farm ku Mchinji
Inu mukamuona mukumusilira
Simukulakwa, munthu ndi wosilirayo
Komano bvuto muli nalo inuyo
Mwati lero ndi lero mufanane naye

(Chorus x 2)

Musamangomuona chonchi uyu (chonchi uyu x2)
Adayamba monyozeka, wabvutika zaka zambiri
Musamangomuona kunjoya, sagona, sapuma
Inu mukuliza mkonono, akukama mkaka Hardworker!

2nd Verse

Achinyamata ambili masiku ano
Sitivomela zomwe moyo watipatsa
Kuba ndalama za boma, cashigeti
Mwagulitsa mitengo yathu kwama Chadi
Mukupha Njobvu kugulitsa Ivory
Lero mukugulitsa munthu mzanu albino
Chili chonse mungofuna chachi dule
Komatu olemera mukanawafunsa

(Chorus x 2)

3rd Verse

Bvuto lomwe tili nalo a Malawi
Timafuna ndalama zitali zitali
Komatu chuma sichibwera pa kamodzi
M'mwenye akulemera ndi ma freezes
Mwafooka, ma Barbershop timawakana
Anzathu ma Burundi akudyera momwemo
Tili ndi zambiritu zolemeretsa
Malo molimbikira tingofuna kuba

(Chorus x 2)

Bridge

Mwapindula chani inu abale inu anzanga
Inu kulemera, kusaukitsa dziko
Chokoma ndi chani kulemera mwadzidzidzi
Koma mapeto ake kukathera kundende

(Chorus x 2)


Songwriters

Lucius Banda

Sharing is cool

From the WorldMobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments
Hits 32755 Plays. | 35164 Downloads.
« Nthungululu Thank You Songs

Recently added songs

Details Votes
Martha Mituka Martha Mituka - Mwayenera
Mwayenera (Gospel)
Mizel Mizel - Wishes (prod. Mc Jones)
Wishes (Rap)
Nomo Cooper Nomo Cooper - Sizokakamiza (Feat. DareDevilz)
Sizokakamiza (Afrobeat)
Dawson Dawson - Ndiwe Okongola
Lilting Rhymes of Lilac (Afro Soul)
DNA DNA - Adzasintha
Adzasintha (Afrobeat)
DNA DNA - Odala
Odala (Reggae)
Young D Young D - Mtengo Wa Malambe (Remix) ft Slessor, Blaze, Marcus, Black Jak, Stich Fray & GD
Mtengo Wa Malambe (Remix) (Hip Hop)
Nicer Nicer - Mkazi Uja (Feat. Chisomo Golombe)
Mkazi Uja (Afro-Pop)
Micky B Micky B - Ulendo Wa Awiri ft Kell Kay
Ulendo Wa Awiri (RnB)
Michael Kasito Michael Kasito - Nyada
Nyada (Gospel)

Join us on Instagram