Vote For This Song

Lyrics

(Verse 1 - Kyc Nyimbo) Dzulo man, zinachitika dzulo Ndinali m' maso koma ngati zakutulo Ndaweruka ku vep ndimwe kamodzi ka botolo komanso magetsi athima ndiguleko kandulo Ndipeze tulo, I had a busy day Ntchito yogwira Monday imapereka busy nde Barman, botolo lakoli Nde ndizabweza mawa Nthawi sikulora ndufunika ku ntchito mamawa Koma, ngakhale kwada ndidzereko kwa Tasha 3 days osamuona koma dzulo anaflasha Amashala yekha amagela ku MIT Ndi waku North anangobwelera geli ku BT Inde ndimankaikira kuti mkaziyu ndi wa zake Manambala okaikitsa amangoti ndi azinzake Nambala ya Peter atha kuiseva Mary Koma ngakhale zili choncho ndayenera ndimuyendere Koma nditangifika, wachibweza chitseko Am like babie ndine Kelvin tsegula ndiloweko Then after 2 minutes, kenako ndakhena Ali mu nsalu koma pambalipa pali ada ena She's like, babie I'm sorry don't leave me Sinapange kalikonse believe me Am like ase, ndisakhale kapolo Muli ndi mwayi sinagwiritse ntchito botolo (Man talking while crying ) Zinandibowa kwambiri, imagine, ada amene anali nawowo, ndi a form 3 And what hurts the most, is that I was the one that paid rent for that house And before that, namvaso nkhani inaso ah (Woman on Whatsapp Voice Note) Thom Thom ukudziwa wapanga zobowa, nakuuza za Olivia ukapezeka zoti uzikamuuza kyc zoona? Mesa nakuuza zoti auzana okha ngati akufuna? Zandinyasa zimene wapangazo nde apapa kyc ndizimuyankha kuti chani? Wachita kunditumizira screenshot ati ineyo nakuuza iweyo that means iweyo unamuuza kyc yo zoti ineyo ndamene ndakuuza eti? Olivia angondikalipira panopa (Verse 2 - Kyc Nyimbo) Ndili ndi babie, inavaya ku S.A Koma nkhani zomwe ndikumva sungadzimvetse My hommie Thom dzulo wandihalla pa whatsapp Ati man mbola am like yeah tathoka wassup? Babie yako Olivia ati ili ndi phaa Wandiuza ndi cousin wake uja Chippa Mwina ukukaikira nde ndingovunga screenshot Am like sh!t koma Mfana wanga anampanga abort Mwina mkona akuika picture ya baby pa DP Akumalusa mkamuuza tumizako ka new pic Kodi bwanji ndimangopleyedwa ngati CD Mtima wanga ukugunda nditha kugwa ndi BP Of course, nane ndinakuplayer ndi Tasha Koma vuto ndiwe unkangondiuza za Russia Kuvaya ku joni unkati ubwera posachedwa I was lonely Nde sindikanapangiraso mwina (Man talking while crying) I had plans with you, I loved you, but mene zililimu, sindingapangireso mwina I just gotta go (Outro) Am heartbroken man Kyc Nyimbo

Sharing is cool

You may also like...Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments

From the World

Hits 4271 Plays. | 3967 Downloads.

Recently added songs

Details Votes
Zephy Oldies Zephy Oldies - Frienemy feat Eminence
Frienemy (Afro-Pop)
Vybez Killer Vybez Killer - My Ganja ft Gibo Lantosi
My Ganja (Dancehall)
Dansa Dansa - Kupewa Ebola
Kupewa Ebola (Afrobeat)
Steve Spesho Steve Spesho - Zifukwa
Special (Gospel)
Steve Spesho Steve Spesho - Ukhale Iwe
Special (Gospel)
Steve Spesho Steve Spesho - Ndifine Odalitsika
Special (Gospel)
Jah View Jah View - Ali Bwanji (Prod. Skill Maker Beats)
Ali Bwanji (Dancehall)
Steve Spesho Steve Spesho - Kaini ft Vj Ice
Special (Gospel)
Steve Spesho Steve Spesho - Sanathane Nane
Special (Gospel)
Steve Spesho Steve Spesho - Ndi Mfiti
Special (Gospel)

Follow Malawi Music on Instagram