Vote For This Song

Lyrics

Amai aduse amai aduse

mphamve ku anthu!

Tisazabalilike siku lo vota*2

amalawi anzanga

mafumu onse agwirizina*2

kwa goliati, kwa mwapesera, ku thabwa, kwa siliya

a group antope!

Onse a coachana!

 

Ndalama zitopezeka, waulesi sazipeza

ngakhale wodyetsa ng'ombe, pano ato pezeka ndi foni

"Hello" akumuziwa!

Asayamika za mai wa, ufiti ali nawo

Asayamika za mai wa, amatowuluka usiku

Chimanga ku admarc chitopezeka chambiri

Asayamika za mai wa ameneyo amawuluka!

 

Chimanga akuchigawa, ali yense amene wavutikisisa

sa sankha chipani


Songwriters

Joe Gwaladi

Bookmark

You may also like...Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Joe Gwaladi's campaign song for Joyce Banda and People's Party. Odi Uko!!!

Comments
Hits 19745 Plays. | 18088 Downloads.
Odi Uko Songs Kwa Goliati »

LIKE MALAWI-MUSIC ON FACEBOOK

FOLLOW MALAWI-MUSIC ON TWITTER