Vote For This Song

Lyrics

Intro Level ikungosintha// Ine simuzanditha// #Hook Eti amaona ngati nditha// Mwanamaaa Eti amaona ngati basi// Mwanamaa Amaonaa ngat nditha ineee// Eti kundikankhila pansi// #verse1 Patali tali game mnaipONYA// Ndikafuna kuombera sindiphONYA// Ndikudya chambo munakadyabe bONYA// Mmakuvani pansi pansi mukutsONYA// Zokamba kamba mbweee// Koma ine ndili phee// Zanga zinayera mbeee// Pano ndikudya chilembweee// Kundikankhira pansi// Inu mmaona ngat basi// Kuchulutsa majelasi// Mtima oipa wa yudasi/ #Hook #verse2 Ondikumbira dzenje adzagweramo yekha// Atcheya samatekeseka// Ine pa easy ndimangoseka// Pa easy ine mmangodekha// Adani mitu zweee// Amafuna ndigweee// Ambuye aponya chingwee// Ndinavala zilimbe// Zokamba kamba mbweee// Koma ine ndili phee// Zanga zinayera mbeee// Pano ndikudya chilembweee// #Hook

Sharing is cool

You may also like...Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments

From the World

Hits 1515 Plays. | 2205 Downloads.

Recently added songs

Details Votes
Khido C Khido C - Zero % ft Binko
Zero % (Hip Hop)
Chris Wapa Eazie Chris Wapa Eazie - Chifukwa (Prod. G Main)
Chifukwa (Hip Hop)
Bathro Bathro - Tanditole ft Blaze & Macelba (Prod. Henwood & Zephy)
Tanditole (Afrobeat)
D.I.C D.I.C - Mpaka ilemba Leka (Prod by Presonus Audio Electronics & Marvel
Leka (House)
Thewz G Thewz G - Mkazi Wanga ft Kell Kay (Prod by Henwood, Tricky Beats & Thewz Exclusive)
Mkazi Wanga (RnB)
Douglass Meleka Khangiwa Douglass Meleka Khangiwa - Sagona Tulo
Sagona Tulo (Gospel)
Douglass Meleka Khangiwa Douglass Meleka Khangiwa - Udzipemphera
Udzipemphera (Gospel)
Douglass Meleka Khangiwa Douglass Meleka Khangiwa - Mukhululuke
Mukhululuke (Gospel)
ITZSAM ITZSAM - YOLO
16 & Hearts (Pop)
ITZSAM ITZSAM - We Going Home (ft. Biggz & Dhone)
16 & Hearts (Pop)