Vote For This Song

Lyrics

#Intro Dontarz waaah Don Nganga Cantiga Yalakwaaa shaaaa Yachimwaaaa Kumamva ena akakuwuza// Sumadziwa mamuna samaluza// Yalakwa game yasuzga// Makolo akakuthoka umati akukuzunza// #Hook Amati angomudyera mpaka phaaa mpaka phaaa (Yalakwa) Iye amati akuchenjera mpaka aaah mpaka eeeeh ×2 #Verse1 Umati zaphweka iwe umudyERE// Wah iwe umati umubere bERE// Iwe umati umudyere ulERE// Yalakwaa shaaa ndi mmene tithERE// Dyere lanulo muona muzIMA// Wah muzafa nazo osakhwIMA// Umafuna kukolora posaLIMA// Kunyanja kunjoya mangochi saLIMA// Daily kumayenda mumdIMA// Tadekhani kumawugwira mtIMA// Mufera pizza tamadyani kwanu nsIMA// Amuna amagagada ndi izi mwaIMA// #Hook #Verse2 Iwe umati basi apa zaphwEKA// Waah mamunatu saadyerEKA// Makolo anakuuza miyendo tatsEKA// Nde ndi izitu lero mwapwetekEKA// Shaa umati ungomudyera bASI// Kufera Gucci iwe ndi AdiDAS// Tadekhani inu takhalani pANSI// Muli mbuu mukufuna madANSI// Kwanu olo njinga kulibe ukufuna wa BENZ// Mulibe kalikonse ukupita ku CHEZ// Nde ndi izitu mwadumphitsapo mwEZI// Bola musakhale mwatengangaso... shaaa// Hook Repeat verse1

Sharing is cool

You may also like...Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments

From the World

Hits 1083 Plays. | 880 Downloads.

Recently added songs

Details Votes
Khido C Khido C - Zero % ft Binko
Zero % (Hip Hop)
Chris Wapa Eazie Chris Wapa Eazie - Chifukwa (Prod. G Main)
Chifukwa (Hip Hop)
Bathro Bathro - Tanditole ft Blaze & Macelba (Prod. Henwood & Zephy)
Tanditole (Afrobeat)
D.I.C D.I.C - Mpaka ilemba Leka (Prod by Presonus Audio Electronics & Marvel
Leka (House)
Thewz G Thewz G - Mkazi Wanga ft Kell Kay (Prod by Henwood, Tricky Beats & Thewz Exclusive)
Mkazi Wanga (RnB)
Douglass Meleka Khangiwa Douglass Meleka Khangiwa - Sagona Tulo
Sagona Tulo (Gospel)
Douglass Meleka Khangiwa Douglass Meleka Khangiwa - Udzipemphera
Udzipemphera (Gospel)
Douglass Meleka Khangiwa Douglass Meleka Khangiwa - Mukhululuke
Mukhululuke (Gospel)
ITZSAM ITZSAM - YOLO
16 & Hearts (Pop)
ITZSAM ITZSAM - We Going Home (ft. Biggz & Dhone)
16 & Hearts (Pop)