Vote For This Song

Lyrics

KAMODZI_DonTarz #Intro Phaa phaa phaa phaaa Wah wah wah Dontarz Lakers Yalakwa yalakwa Eti Warge #Hook Kamodzi waah yooh// kanali kamodzi// Eti kamodzi// Sikawiri kanali kamodzi// #1stverse Koma zoona ndikumva panoZI// Makolo ake asanduka apongozi// Shaaa izi nde ndizangozi// Waaah eti basi kamodzi// Yalakwa game yapotoka// Mmayesa bodza mmene amandithoka// Kamodzi kokha awa ndi matsoka// Kamodzi pompo kutora Joker// Hook #2ndverse Ndekuti kapena ineyo ndikatswiri// Kapena ndimadya chinangwa chambiri// Waah apa yalakwa kwambiri// Eti kamodzi osatiso kawiri// Zomwezi ena mpaka kwa Bushiri// Kusala kudya ena kukwera phiri// Ine kamodzi osatiso kawiri// Waaah ndadzionongera mbiri// Hook #3rdverse Ndekuti ineyo ndimatha// Koma pano nde ndili ndi mantha// Mdala yake pano yakwiya// Mkanadziwa ndikanangosiya// Shaaa ndingothawa apapa// Braz yake ikuti indichapa// Mdala yake ikuti indikhapa// Apapa nde ndachilapa// Hook.....

Sharing is cool

You may also like...Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments

From the World

Hits 730 Plays. | 629 Downloads.

Recently added songs

Details Votes
D.I.C D.I.C - Mpaka ilemba Leka (Prod by Presonus Audio Electronics & Marvel
Leka (House)
Thewz G Thewz G - Mkazi Wanga ft Kell Kay (Prod by Henwood, Tricky Beats & Thewz Exclusive)
Mkazi Wanga (RnB)
Douglass Meleka Khangiwa Douglass Meleka Khangiwa - Sagona Tulo
Sagona Tulo (Gospel)
Douglass Meleka Khangiwa Douglass Meleka Khangiwa - Udzipemphera
Udzipemphera (Gospel)
Douglass Meleka Khangiwa Douglass Meleka Khangiwa - Mukhululuke
Mukhululuke (Gospel)
ITZSAM ITZSAM - YOLO
16 & Hearts (Pop)
ITZSAM ITZSAM - We Going Home (ft. Biggz & Dhone)
16 & Hearts (Pop)
ITZSAM ITZSAM - Underrated ft. Biggz
16 & Hearts (Pop)
ITZSAM ITZSAM - Tama
16 & Hearts (Pop)
ITZSAM ITZSAM - Star Crossed ft. Vitu
16 & Hearts (Pop)