Vote For This Song

Lyrics

Verse 1 Lero ikhala finals Undiuze umaona chani mwa ineyo Ukamanditreater chonchi Umati ndine ndani kwa iweyo Kodi mesa amati m`modzi mwa ifeyo Anachokera kunthiti ya nzache Ndikudabwa kuti m`modzi mwa ifeyo Salabadira mkomwe zanzache Bridge Zizikomera mbuzi kugunda galu chikondi chanji darling Kukhumudwitsa nthiti mtima uli m`malo umakwanitsa bwanji darling Chorus Kukonda iweyo, sikuti ndikupusa ayi Ndikamakupepesa, sikuti kusatira khusa zako Koma mtimaaa, mtima wathu uzatipusitsa ife Abale chikondiii, chikondi chathu chizatipwetekesa ife Tisafele mphathi Verse 2 Ayi ndisaname sweet inu, inu mwanditora pamudzi pano Ngati kuti mwina ine ndilibe kwathu Mwanditora pamudzi pano Ine ndikalakwa ndimapepesa Koma ayi mpakana suspension Mukalakwa ndimamvetsetsa Munthu sangalakwire mtengo Bridge Zizikomera mbuzi kugunda galu chikondi chanji darling Kukhumudwitsa nthiti mtima uli m`malo umakwanitsa bwanji darling Chorus Kukonda iweyo, sikuti ndikupusa ayi Ndikamakupepesa, sikuti kusatira khusa zako Koma mtimaaa, mtima wathu uzatipusisa ife Abale chikondiii, chikondi chathu chizatipwetekesa ife Tisafele mphathi Bridge Usazuze mtima Usazuze mtima Usavulaze mtima wa ine Usazuze mtima Usazuze mtima Usazuze mtima Usavulaze mtima wa ine Usazuze mtima Kodi mesa amati m`modz mwa I ifeyo Anachokera kunthiti ya nzake Ndikudabwa kuti m`modzi mwa ifeyo Salabadira mkomwe zanzake Chorus Kukonda iweyo, sikuti ndikupusa ayi Ndikamakupepesa, sikuti kusatira khusa zako Koma mtimaaa, mtima wathu uzatipusisa ife Abale chikondiii, chikondi chathu chizatipwetekesa ife Tisafele mphathi

Sharing is cool

From the WorldMobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments
Hits 15916 Plays. | 10424 Downloads.

Recently added songs

Details Votes
Eagle Sight Eagle Sight - Madam Anga ft Tay Dee (prod by King Duda)
Madam Anga (Hip Hop)
Prince Kho Prince Kho - Too Loud
Too Loud (Hip Hop)
I Cent I Cent - Poto Ndi Mkati ft M.O.D
Poto Ndi Mkati (Afrobeat)
Sir Jent Kago Sir Jent Kago - Silence (Prod by Warge)
Silence (Dancehall)
C-Triz C-Triz - Personality [Prod. Dkez Walker]
Personality (Reggae)
Jungle Jex Jungle Jex - SizaNormal (Prod. Mkadyman & Jay Kay Beats)
SizaNormal (Afrobeat)
Mr GB Mr GB - Matope
Matope (Afrobeat)
Jack B Jack B - Musazipope ft Mr GB
Singles (Dancehall)
Deevah Di Warthog Deevah Di Warthog - Sangayamike ft Ambassador
Sangayamike (Dancehall)
Archaida Universe Archaida Universe - Wandekha (Malinga x Kay Stevoh x Govana x Chargie)
Wandekha (Dancehall)

Join us on Instagram